Project Hope     home >>stonecroft>> utumiki wachi afrika
Utumiki wachi Afrika
Women's Empowerment Program
Sports Bible Club
Living Water Bible Club

CHITSANZO CHABWINO CHA UTUMIKI WACHI AFRIKA

Utumwi wachitsanzo wachifilika watsimikiza kuti nkwabwino kugawa kuti muchulukitse ndinso kuchulukitsa nkwabwino kuposa kuonjezeera

1. Chitsanzochi chamu Africa chiidzayambitsidwa kaye poyamba mu Tanzania kudzera ku (ATBS) cholinga chake chenicheni ndikuphunzitsa a Stonecraft ziphunzitso za mu baibulo kwa olondolera. Pogwiritsa ntchito kanema wa ziphunzitso ndinso bukhu la olondolera lamanja la ziphunzitso, tidzapatsa chitysogozo kwa azibusa omwe akupanga nawo maphunziro awo tsopanowa pa (ATBS) ku Tanzania komanso Malawi ndi Zambia. Azibusa amenewa adzakhala oondolera oyamba mu Tanzania Mulungu akalolra. Adzapatsidwa aliyense limodzi mwa ma baibulo la mgwirizano swahiri chipangano chatsopano, limodzi la bukhu lawolondolera ndi ndongosolo lakle ndi mabaibulo a ziphunzitso zowelenga mu ndime ya utatu woyera, mkamaka khumi a Yesu ndiye ndani? Kenako khumi a Mulungu ali ngati chiyani? Ndilotsiriza lake la kodi Mzimu woyera ali kuti? Khumi nawo.

2. Azibusa adzaqtengera uthengau ku mipingo yawo kumadela kwawoko ndikupeza mzimayi wachangu pa ntchito ya mulungu kaya ndimtsogoleri wa azimayi, pogwiritsa ntchito kanema yophunzitsirayo ndi bukhu la wolondolera la Stonecroft mu Africa la mmanja, adzaphunzitsa olondolera m’mipingo wamba yoyambira kwawoko, ndiye m’usayo mgwirizanitsi woyang’anira mayiyo

3. Wolondoler watsopano adzapatsidwa mabaibulo atsopano khumi achipangano chatsopano, bukhu la wolondolera mwadongosolo la Stonecraft, ndi khumi la mabukhu ophunzira baibulo a Stonecraft a kodi Yesu ndi ndani? Onse otanthauzilidwa mu chiphunzitso cha kwawo chomwe ndipo, adzafuna amayi asanu a mum’pingo momwemo oyenera kulondolera bwino kuti ayambe kutenga gawo. Mmodzi mwa amayi olondolera osankhidwawoatha kubweretsa mzawo m’modzi, makamaka opemphera naye ku gulu laziphunzitso za baibulo, ngati ziphunzitso za baibulo zatha adzaphunzitsa azimayi asanu osankhidwawo kuti akhale gawo achitatu la wolondolera a Stonecraft mogwiritsa ntchito kanema wophunzitsilayo ndimabukhu ophunzitsilayo ndi mabukhu ophunzilira ophunzilira baibulo a Stonecroft a m’manja

4. Adzakhala mgwirizanitsi kuwonelera olondolera asanuwo

5. M’usa adzakhala mgwirizanitsi wankulu woonelera ntchitozo.

6. M’modzi wa olondolera asanuwo pamodzi ndi anzawo opemphera nawowo adzapeza muntu wachangu m’modzi kuchoka pa mpingo wawo mwina mdelaro ndi winanso woyenera woti atha kulondolera bwino kuchoka ku mpingo wina mopmvana ndi abusa ake kumuloleza.

7. Pamodzi amayi anayiwa adzalimbikitsa anthu omwe Sali okhulupilira kulowa mgulu ophunzira atsopanowa anthu awiri aliyense. Kumbukani maphunziro a baibulowa ayenenera kusapitilira anthu okwana khumi.

8. Ngati ziphunzitso za baibulo za Yesu ndiye ndani? Zatheka ayenera kuphunzitsa amayi awiriwo (m’modzi wochoka kumpingo wake winayo ku mpingo wina) kuti adzakhale gulu lachinayi la wolondolera a Stonecroft. Wopemphera naye mzakeyo adzakhala naye kuphunzitsa mkalasi kuphunszitsa ziphunzitso zina za baibulo za muphunziro la utatu woyera.

9. Dongosololi limatsatidwanso ku mipingo ina yomwe yaikidwa nawo mu ndondomeko imeneyi

10. Ngati pali mafunso ena onse amene olondolera sangathe kuyankha ayenela kuwapeleka kwa mgwirizanitsi amene ayenera kukhal mbusa.

11. Pomwe nthawi ikupita agwirizanitsi ena adzakhala akuphunzitsa ngati mgwirizano ukukula kanema adzakhala akugwiritsidwa ntchito kwa ziphunzitso za wogwirizanitsa

12. Kumbukirani kugawa kugawa kuti muchulukitse.

13. Kuchulukitsa nkwabwino kuposa kuwonjezera

“muyenera kukhala a tcheru, kuima njii mu chikhulupiliro, khalani olimbika, amphamvu. Muchite ntchito zanu zones mucikondi”
1 Akorinte 16:13-14

 
 

 

 
 
Copyright ©  2023 www.UnitedCaribbean.com. All rights reserved. Disclaimer Click to Contact us