Project Hope     home >>stonecroft>>mfundo za stonecroft paziphuinzitso za m'baibulo>>ndondomeko ya kuphunzila
NDONDOMEKO YA KUPHUNZILA
Women's Empowerment Program
Sports Bible Club
Living Water Bible Club

NDONDOMEKO YA KUPHUNZILA OLONDOLERA ZOMUYENELEZA OLONDORELA
Zofunikila za olondolera ndi kusogolera ndi kulondolera ziphunzitso zabaibulo.
Pomwe olondolera akugwira nthchitoyi ali ndi mwayi otensela dera lawo poyambitsa kuti enatso akhale ndi chiyanjano chawo ndi Yesu Khristu

WOLONDOLERA ZIPHUNZITSOZAM’BAIBULO WA STONECROFT

  • Amapemphelera nthawi ndi nthawi yemwe akhale muziphunzitso za baibulo
  • Amayamba ziphunzitso za Baibulo ndi pemhero
  • Otsogolera baibulo wa Stonecroft amaphunzitsidwa ndi otsogoza kukhazikitsa ziphunzitso za baibulo amakhala woziwitsidwa ndikukhonzelekesedwa munjila zopititsa patsogolo la luntha lake ngati wolondorera ndi mtsogoleri wake.
  • Wolondolera amatsatila mfundo zones za Stonecroft kuphunzitsa baibulo ndipo oyenela kuziwisa otenga mbali momwe angayenele kukhala ochita ndi umozi pagulu posatila zotsogoleza zomwe zayikidwa muchiwonetselo ichi.
  • Amakhozeketsa gulu lake kuyang’ana maso pamafutso a ziphunzitso zabaibulo
  • Amapeleka mwayi kwa ophunzila ndi kutenga mbali kuti aziwe za momwe uliri utumiki wa Stonecroft ndikuwuziwitsa kwa otenga mbali mderaro za mwayi oti iwo angalumikizane ndi amdera lina.
  • Amayetsesa kufuna kuwalondolera otenga nawo mbali kupeza kupeza mayankho kwa malutso azikhulupiliro zaw
  • Zokambilanazo zimalimbikitsidwa p-okhapo pomwe baibulo limanena osati kuyima pamene mpingo ndi zikhulupiliro zawo zimaphunzitsa.
  • Amafunitsa kusayang’ana zomutsokoneza nditso kumutalikitsa kuzinthu zochokela ku zomwe ziphunzitso, zochitika mmadera lamuzabndale ndi zina zomwe anthu kapena mipingo amakangana.

WOLONDOLERA AKHALE NDI IZI:-

1. Wolondolera akhale ndi chiyanjano ndi Yesu Khristu
2. Akhale ndi chikhumbo chofuna mphavuyo sintha moyo yam au a mulungu
3. Akhale wogwizana ndi mfundo ndi ndondomeko za ziphunzitso za baibulo za Stonecroft
4. Amatolerana ndi kugwila bwino ntchito ndi anthu ena.
5. Ali ndi chifuniro chotengela anthuena kuziwa mau amulungu ndi kuwakulitsa muuzimu ngati akhristu.

KUSANKHA OLONDOLERA WOYENERA WAZIPHUNZITSO ZA BAIBULO
KASANKHIDWE KA OLONDOLERA

In Africa, unless the Pastors catch the vision it is very difficult to introduce the programme into the churches, schools or orphanages associated with these churches. So we have identified Pastors from throughout Africa. These Pastors in Africa are part of the Africa Training Bible School and will be trained to be Guides, they will then train their key women within their local church.

Makamaka azibutsa omwe amaphunzitsidwa kukhala olondolera angapeze ena muderalo moganizila, mwapemphelo ndi dongotsolo, kusankha athu oyenela ngati olondolera mudera lawo ndipo kupeleka mwayi wakukula mochuluka wa ziphunzitso zamubaibulo za Stonecroft

Nchoyenela kuyang’ana zoyeneleza wolondolera yemwe angasatev bwino malo ofunikila poganizila anthu otumikila ngati olondolera

(1) Kupemphera pasanafike tsiku la ntsonkhano lokumanira ndi ofunawo kupempha mulungu kupeleka mzeru kwa inu ndi ofunawo ndinso Mzimu wa chiziwitso mogwilizana ndi udindowo.

(2) Kupeza nthawi yoziwana bwino lomwe muyenela kuziiwitsa za ziphunzitso za baibulo za Stonecroft ndi utumiki wake ngati nkoyenera

(3) Muyang’anile mwamasdera munthawi yazitsankho omwe ali mkati mwa folamu yofutsila yaziphunzitso za Stonecroft.
• Pelekani chiziwitso pa utumiki wa Stonecroft muwayang’anize ofuna kukhala wotondolera ku :-
1. Ziphunzitso za Stonecroft bukhu la banja
2. Fikani mu stonecroft corporate pa internet yawo stonecroft@org kuti muziwe zambiri
• Mufutse olondolera kuti anene mwatsatane tsatane momwe anakhulupilira Yesu Khristu payekha pa chipulumutso chake ndipo apelike mavesi a m’baibulo omwe akusimikiza kuti za ukadaulo pa chikhulupiliro chake.
• Mufuse olondolayo kufotiokoza satane satane m’mene angayankhile za mbiri yokuza Yesu Khrisu
• Muziwepo kwa olondolerawo chomwe chinawakopa kugwira ntchito ndi Stonecroft mziphunzitso a baibulo.
• Muyang’ane kufunitsisa kwawo ogwila ntchito ndi zikhulupiliro zikhalidwe ndi zipembezo zosiyana-siyana.
• Muwafuse olondolerawo zina zimene iye amachita ndiukadaulo wake potsogoza ziphunzitso za baibulo
• Muwonesese ndiwoziwitsisa mfundo za Stonecroft muziphunzilo za baibulo ndi dongotsolo la chikhulupiliro chawo.
• Oyenela kukulondolera ayenela kuwerenga ndikumvetsa mfundo za Stonecroft pakusasokonezeka.

Zofunikira Zoyang'anira
 
 

 

 
 
Copyright ©  2023 www.UnitedCaribbean.com. All rights reserved. Disclaimer Click to Contact us