Project Hope     home >>stonecroft>> ndondomeko yolondolera >>nthawi yoyandikira ziphunzitso za baibulo
NTHAWI YOYANDIKIRA ZIPHUNZITSO ZA BAIBULO.
Women's Empowerment Program
Sports Bible Club
Living Water Bible Club

NTHAWI YOYANDIKIRA ZIPHUNZITSO ZA BAIBULO.

Zofunikira zina zochepa:
Uyenera kubvomelezedwa ngati wolondolera wa Stonecroft momaliza folomu yofunsira ya ziphunzitso za Baibulo za Stonecroft yomwe yatanthauzilidwa muchilankhulo cha chiswahili kwa ofunsila a Tanzania.

Tikufuna kudziwa udindo wanu ndi mbali yanu pa mpingo.

Tikufuna kudziwa ngati mwawerenga mfund za zautumiki wa Stonecroft ndi mfundo yachikhulupiliro kuti palibe chomwe mwakhuzidwa nacho

ZOFUNIKIRA PA ZIPHUNZITSO

1. Bukhu la chiyambi utatu woyera lophunzilira lotanthauzilliqwa mu chiswahiri litha kupezeka kuchoka ku likulu la (ATBS) Mbeya, Tanzania.
2. Mabukhu ophunzilira atha kutengedwa kuchoka ku Mbeya, Tanzania.
3. Baibulo la chiswahiri mgwirizano litha kupezeka kuchoka ku bungwe la mabaibulo la Tanzania.
4. Kodi mungazikhulyupilire izi? Latanthauzilidwa mu chiswahili ndipo litha kupezeka ku likulu lawo la (ATBS) ku Mbeya, Tanzania.
5. Makhadi a chidziwitso atanthauzilidwanso ndipo atha kupezeka ku likulu lawo la (ATBS) ku Mbeya, Tanzania.
6. Fomu ya wolumikiza (wolondolera) lofunsira za uphunzitsi wa baibulo titha kupezeka ku likulu la (ATBS) ku Mbeya, Tanzania.

Mupeze mala oyenelera a ziphunzitso zamubaibulo, muganizile zohita maphunziro mnyumba, tchalitchi, mkalasi pa tsiku loweluka, mwina panja pa mthunzi wabwino pansi pa mtengo.

KUKHONZEKERA ZIPHUNZITSO

Mumalizitse ziphunzitso polemba mayankho mu bukhu lophunzitsira musanawerenge bukhu la ndondomeko. Izi zikuthandizani kumvetsetsa malingaliro omwe ena atadutsemo kukafikira mayankho oyenelera

Muphunzire kuwerenga ziphunsitso mokweza ngati kungakhale koyenelera. Musindikize malembo ofunikira ndi mau ena apadera omwe angakuthandizeni kumvetsa bwino lanu kugulu.

Under normal circumstances lessons should not exceed 1 – 1 1/2 hours particularly if the Bible Study is part of the Africa Women’s Empowerment Program (AWEP) because the ladies will have to leave and start their Vocational Training Lessons.
• At the same time as AWEP students are enjoying their Bible Study their child will be attending their PowerClub to be trained in the ways of God through Africa Bureau of Children’s Discipleship Curriculum including the Grow and Go curriculum alongside the Drop of Hope Organic Kitchen Garden project as well as the 'Kids in Ministry International' curriculum and other children’s ministry including Kids Evangelism and Youth Discipleship Programs.

• Initially the locations will be:
Tanzania – Africa Training Bible School (ATBS) – Mbeya Tanzania (Swahili)
Uganda – Hope Community Centre, Kampala (English)
Malawi – Africa Training Bible School (ATBS) – Uluwa and Vulwa, Malawi (Chichewi)
DR Congo - Africa Training Bible School (ATBS) (French)

NTHAWI YA ZIPHUNZITSO

Nthawi zonse yambani maphunziro ndi pemphero, ngati wina wake wanena pempher, muganizile kuti gulu lilembe pa zopemphelerapo pa tsamba la bukhu lophunzilira kumapeto ngati chikumbutso kudzapemphelerapo mkati mwa sabata.

Ngati pempho ndilofunika msanga, muziikepo kuyamba kwa ziphunzitso mupemphero lotsegulira.

Mukumbukire kuti pachiyambi pa phunziro la gawo lirilonse monga yesu ndiye ndani? Munthu yense ayenera kulemba mayankho ake mubukhu lophunzilira pa phunziro loyambilira. Pazotsatira zina zophunzilira mulimbikitse gulu kumaliza maphunziro pakuyamba kwakukumanako potsindikiza mayankho mubukhu lophunzilira musanafike kukalasi.

Muerenge ndikupeleka uthenga mubukhu lolondoza ndondomeko mwapamwamba moyang’ana maso bwino lomwe kwa ophunzira. Wolondolera akuphunzira nawo limodzi ndi gulu kuli oyenera kukhala kadaulo pa baibulo.

Wolondolola amayi kumveka bwino ndi mulingo wa ziphunzitso potsatira izi:-
• Kuyamba ndikutsinzina panthawi yake, kumbukirani zambiri za ziphunzitso zizikhala zophatikizana ndi ndondomeko ya amayi kupatsidwa mphamvu ya Sstonecroft, ndiye, azimayi ayenera kuchoka ndikupita kuziphunzitso zantchito yamanja pamapeto pake.
• Gwiritsani ntchito bukhu lolondoza ndondomeko ndi baibulo lwa chiswahiri mgwirizano ndi ena mwa ma baibulo oyenera omasulidwa bwino ku maiko ena, sipafunikanso zipangizo zina za padera..
• Limbikitsani wina aliyense kutenga nawo mbali muzokambirana, kusalora kuti wina akulamulira kwambiri, muyenera kukhala okoma mtimapomwe mukulibikitsa ena kutenga nawo mbali posamukhumudwitsa yemwe akutenga nawo mmbali kwambiri.

Muyike maso pakuphunzira za yesu, osati osati ziphunzitso zawamba, za ndale kapena zochitika mdera, mafunso aziphunzitso za wamba amatha kutengedwa bwino panthawi inayoyenera bwino.

Nthawi zones yang’anani omwe ali mgulu omwe angadzakhale olondolera ziphunzitso za mtsogjolo.

Ngati wolondolera mukhale chitsanzo choawonetsa tsankho. Muletse anthu kuleka kukambirana zinthu zimene siziyenera kukambidwa pa gulupo monga mikangano ya kunyumba kuwonjezera pa zochit za pa gulupo. Mupemphere ndi anthuwo ndikuwalimbikitsa kufuna chitsogozo cha Mulungu.

Pomaliza pa dondosolo la azimayi kulandira mphamvu a Stonecraft, aliyense amene angachite kulondolera bwino asankhidwe ndikuphunzitsidwa kupeleka mwayi kwa omwe amaliza maphunziro kubwelera kumanyumba kwawo potenganso ndi ziphunzitso zawo kumadera kwawoko.

Mufunse otenga nawo mbali za omwe angawaitane kumaphunziro ena baibulo. Muwalimbikitse kupemphelerana mayina wina ndi mzake.

ZOYENERA KUDZIWA (OSAIWALA)

  • Ngati muli olephera kuwerenga maphunziro a baibulo pazifukwa zina, wina obvomelezeka kapena wophunzira bwino wapambali ayitanidwe kutenga malo anu.
  • Simuli ololedwa kupeloeka bukhu la ndondomeko yolondolera kwa membala wina wa mkalasi lanu.

Azimayi Kupatsidwa Mphamvu
 
 

 

 
 
Copyright ©  2023 www.UnitedCaribbean.com. All rights reserved. Disclaimer Click to Contact us