Project Hope     home >>stonecroft>>mfundo za paziphuinzitso za m'baibulo>>buku lophunzitsira lotsogolera
YESU NDI NDANI? - Buku Lophunzitsira Lotsogolera
Women's Empowerment Program
Sports Bible Club
Living Water Bible Club

YESU NDI NDANI?

Buku Lothandiza

Chitsogozo chotsogolera
Yesu ndi ndani?

Chiyambi

Mumadziwa chani za Iye? Ndizimene maphunzirowa akufotokoza—
K udziwa chenicheni cha chimene Yesu ali,
C hifukwa chani anabwera pa dziko la pansi,
kubwera kwake kuli ndi tanthauzo lotani kwa ife,
T idzamuona Iye.

Timamudziwa Mulungu kudzera mu zimene Yesu adachita pamene anali pa dziko lino lapansi. Kuti tikhale pa ubale weniweni ndi Mulungu, choyamba ndikofunika kum'ziwa Yesu.
Pachifukwa ichi, tinaganiza kuti Yesu ndi Ndani? adzikhala maphunziro oyambirira mu mdandanda wa maphunziro athu:

Yesu ndi Ndani?, Mulungu ndi Wotani?, ndipo Mzimu Woyera Alikuti?
Pamene mukuphunzira za Yesu, Mwana wa Mulungu, mumudziwe ndikulandira uthenga umene anaubweretsa pa dziko la pansi.

Mulungu akudalitseni ndi bvumbulutso latsopano ndi lakuya la Mwana wake wodalitsika, Mpulumutsi, Mbuye Yesu Khristu.


“Koma zalembedwa izi kuti
mukakhulupiriree kuti Yesu ndiye
Khristu Mwana wa Mulungu, ndi
kuti pakukhulupirira mukhale nawo
moyo m'dzina lache.

Yohane 20:31

Lucille Fern Sollenberger

 

 
 

 

 
 
Copyright ©  2023 www.UnitedCaribbean.com. All rights reserved. Disclaimer Click to Contact us