Project Hope     home >>stonecroft>>bukhu la m'manja>>mbili ya stonecroft
MBILI YA STONECROFT
Women's Empowerment Program
Sports Bible Club
Living Water Bible Club

MBILI YA STONECROFT

Leroli, kufikila kwa utumikiwu kwafikila padziko lonse ndikukhuza miyoyodzikwi dzikwi pa chaka chimodzi. Koma mbiri yake ya Stonecraft inayamba mochepa kwambiri- ndi mzimayi m’modzi-Helen Duft Baugh- Mzimayi wachikhulupiliro chosagwedezeka mzimayi wapemphero, muzimayitso wazifuno wa zozama za tsogolo lamuyaya la ena.

Kuchoka muchiyambi chochepacho muchaka cha 1938 magulu ena otero la bizinesi za amayi anakhazikitsidwa padziko lonse. Muchaka cha 1944 Miss Mary E. Clark, wabizinesi wakale ndipo ntumiki wankulu ku Main, anavela kuyitana kwa Mulungu nalumikizana ndi Mrs Baugh kuthandiza kutsogolera kwa bungwe lokulira kulira la uthenga wabwino ndi utumikili onse ndiponso madela osiyana siyana amoyo wawo.

Mu chaka cha 1952, Mulungu mwachitsomo anapeleka malo mdela la Kansai City Missoiri, kuti likhale ngati likulu. Dzina lamalowo Stonecraft kutanthauza kuti “Nyumba ya mwala”, ndilo linatengedwa ngati dzina la utumikiwu ndipo limatikumbutsa kuti Yesu ndiye maziko olimba ndi mwala wapangodya wamphamvu za utumiki.

Kwa zaka zokwanila makumi asanu ndi awiri (70yrs) Mulungu adalilika ndi kuteteza kuthandiza ndiposo kulondoza ntchito za utumiki wa Stonecraft. Mu mumukhalidwe wosintha sinthawu, zinthu ziwili zakhala zosasunthika kuzipeleka kwathu muapemphelo ndikufalitsa uthenga wabwino.

Stonecraft mwaposachedwa yagulitsa malo amenewa ndikusuntha ku malo ena ocheperapo ama office awo kupeleka mpata wopitilirabe ndi kugwilitsa ndarama zotsatila pa ntchito yolarika ndikufalitsa uthenga wabwino.

Utsogoleri wa Stonecroft

 
 

 

 
 
Copyright ©  2023 www.UnitedCaribbean.com. All rights reserved. Disclaimer Click to Contact us