Project Hope     home >>stonecroft>>utsogoleri wawo wa stonecroft>> dongosolo lachikhulpiliro cha stonecroft
DONGOSOLO LACHIKHULUPILIRO CHA STONECROFT
Women's Empowerment Program
Sports Bible Club
Living Water Bible Club

DONGOSOLO LACHIKHULUPILIRO CHA STONECROFT

  • Utumiki wa Stonecroft umakhulupilira muuzimu, wonsewofikapo kwathunthu ndi kulimbikisidwa kwa m’malembo-baibulo ndilopanda kalema ndipo ziphunzitso ndi ulamuliro wake ndizofikapo zapamwamba ndimapeto.
  • Timakhulupilira mu utatu woyera wa uzimu, Mulungu tate Mulungu mwana ndi Mulungu Mzimu woyera.
  • Timakhulupilira umunthuwa Umulungu, umunthu ndi umulungu wa (Yesu Khristu ndi Mulungu ndi Mulungu wozionetsera ku thupi) wobelekedwa ndi muzimu woyera , mulungu yese, Munthu yense umnthu wa nzimu woyera.
  • Timakhulupilira kuukitsidwa kwa yesu khristu, kuti thupi lake linaukitsidwa kwa akufa, mwamalembo, ndipo anakwela kumwamba anakhala kudzanja la manja la Mulungu ngati wotinenera zabwino okhulupilira.
  • Timakhulupilira kuchimwa kwa munthu kuti munthu yese anabadwa ndi uchimo, ndiyeso yeka mombolo ku uchimo.
  • Timakhulupilira kukuyeletsedwa, kuti Yesu anadza ngati nsembe ya ochimwa pamaso pa Mulungu, pamene anakhetsa mwazi wake ngati dipo kuuchimo wadziko lonse lapatsi.
  • Timakhulupilira kufunika kwa kubadwa mwatsopano
  • Chipulumutso ncha chisomo, kuzela muchikhulupiliro osati ntchito zabwino mu umoyo wamunthu wokhulupilira.
  • Timakhulupilira muukuwukisidwa koonekelatu kwa thupi kwa onse ochimwa ndi oyela mtima.
  • Timakhulupilira mukulalikira uthenga wabwino kudziko lapasi-chofunika chahikulu cha Mulungu ndicho kuti anthu ake mumbadwo uno alalikire uthenga wabwino kwa cholengedwa chake (Munthu) aliyense.
  • Timakhulupilira kubweleranso kwake kwachiwirikwa yesu khristu monga mwa malembo.

Phunziro la Baibulo

 
 

 

 
 
Copyright ©  2023 www.UnitedCaribbean.com. All rights reserved. Disclaimer Click to Contact us