Project Hope     home >>stonecroft>> buku lamanja la africa
Stonecroft- Buku Lamanja la Africa
Women's Empowerment Program
Sports Bible Club
Living Water Bible Club

KAYALIDWE KAZAMKATIMU,

ZAMKATI

STONECROFT (CHOLINGA CHAWO NDIMASOMPHENYA AWO)

•  MBIRI YAWO YA STONECROFT

•  USOGOLERI WAWO WA STONECROFT

•  DONGOSOLO LA CHIKHULUPILIRO CHA STONECROFT

•  ZIPHUNZITSO ZAMUBAIBULO ZA STONECROFT

•  ZOZIWIKA NAZO ZENIZENI

•  ZODZIWIKAWIKA NAZO ZENIZENI

•  ZOPHUNZILA ZOYENELERA

•  KUSANTHULA KWA ZIPHUNZITSO ZA BAIBUKLO

•  DONGOSOLO LA ZIPHUNZITSO ZA OLONDOLERA

•  ZOMUYENELEZA WOLONDOLERA

•  KASANKHIDWE KIA WOLONDOLEDWA

•  KUSULA WOLONDOLERA

•  MALANGIZO KWA WOLONDOLERA

•  YOYANDIKILA ZIPHUNZITSO ZA MBAIBULO

•  KUKHONZEKELA ZIPHUNZITSO ZABAIBULO

•  NTHAWI YA ZIPHUNZITSO ZA M'BAIBULO

•  STONEROFT KUZAMITSA AZIMAYIMAYI (NDONDOMEKO)

•  ATUMWI ACHIFIRIKA ACHITSANZO

BUKHU LA M'MANJA LAZIPHUNZITSO ZAM'BAIBULO LA STONECROFT AFRICA

CHOLINGA CHA STONECROFT NDIMASOMPHENYA AWO

Cholinga cha stonecroft ndi utumiki wawo ndi kutengela ndikulimbikitsa azimayi kuti afikile madela awo ndi uthenga wa Yesu Khristu ndi kulemekeza Ambuye Yesu Khristu, ndi kumupanga Ambuye Yesu kudziwika polalika uthenga wa chipul;umutso wa M'baibolo

MASOMPHENYA AWO:

Masompheya a utumiki wa Stonecroft ndikupeleka utsogoleri wapadziko lonse pofikila azimayi ndi Yesu Khristu.

A Stonecroft ndi utumiki wawo amasula azimayi ndi kuwalimbikisa kuti amuziwe Yesu Khristu kwa ena

Kulalikira ndiye gwero lathu. Mongatso kwa utumiki wina uliwonse ndi choncho. Khumbo lathu ndikufikila mzimayi wamsinkhu uliwonse ndi nkhope iliyose ndi uthenga wa Yesu Khristu.

Pemphero ndi maziko ndi nkanamila ya china chili chose timachichita. Yesu anati " kopanda ine simungathe kuchita chilichose " Jonane 15:5

Kudalila mulungu kufuna chitsogozo chake, ndiponso mdalitso wake ndichofunika zedi.

Utumwi ndi gawo la dongosolo la utumiki wa uthenga wabwino. Momwe azimayi akukhalira ukristu wake, moti tikupeleka mwayi ndi zipangizo kuthandiza iwo kukula muchikhulupiliro ndiye keneko iwonnso atengele anzawo kuchiyanjano ndi khristu.

Kusula azimayindi utsogoleri ndicholinga chathu china chautumiki wanthu. Kuthandiza azimayi kuzindikila ndi kukulitsa mphatso zomwe mulungu wawapatsa. Kuwazika kuti akhale atsogoleri oyenera omwe angasinthe pakhomo, Mudzi dela dziko lawo, nditso dziko lonse kwa Yesu Khristu.

Zolinga zaziphunzitso zabaibulo za Stonecroft ndizo kulalikila ndi utumwi ziphunzitso zosavuta kulondolazo zammamagulu aang'ono ang'ono zimalimbikitsa moyo wauzimu kuti akule kwa nkhala kale zokhulupilika komano omwe akuphunzila baibolo kumene.

A Stonecroft amagawa uthenga wabwino kwa amayi padzikolonse, ozipeleka oposa 25, 00 osulidwa bwino, nthawi ndi nthawi amayitanila azimayi mdera awo kuti ayambe ubale wawo nd Mulungu wadzikolonse kuzela mwa mwana wake Yesu Khristu.

Wozipeleka mudziko la United States ndiwo mayiko opyola makumi atatu (30) amagwilitsa ntchito zipangizo zofikila za Stone craft ndinso ziphunzitso za baibulo kugawa uthenga wabwino kwa zaka zoposela (75) azimayi a Stonecraft adalira pemphelo ngati chida chotukulila utumiki.

Stonecraft nd bungwe lapadziko lonse, lopanda kuyimila mpingo, ndipotso lopanda zopindula kuchuma.

MBILI YAKE YA STONECROFT

Leroli, kufikila kwa utumikiwu kwafikila padziko lonse ndikukhuza miyoyodzikwi dzikwi pa chaka chimodzi. Koma mbiri yake ya Stonecraft inayamba mochepa kwambiri- ndi mzimayi m'modzi-Helen Duft Baugh- Mzimayi wachikhulupiliro chosagwedezeka mzimayi wapemphero, muzimayitso wazifuno wa zozama za tsogolo lamuyaya la ena.

Kuchoka muchiyambi chochepacho muchaka cha 1938 magulu ena otero la bizinesi za amayi anakhazikitsidwa padziko lonse. Muchaka cha 1944 Miss Mary E. Clark, wabizinesi wakale ndipo ntumiki wankulu ku Main, anavela kuyitana kwa Mulungu nalumikizana ndi Mrs Baugh kuthandiza kutsogolera kwa bungwe lokulira kulira la uthenga wabwino ndi utumikili onse ndiponso madela osiyana siyana amoyo wawo.

Mu chaka cha 1952, Mulungu mwachitsomo anapeleka malo mdela la Kansai City Missoiri, kuti likhale ngati likulu. Dzina lamalowo Stonecraft kutanthauza kuti "Nyumba ya mwala", ndilo linatengedwa ngati dzina la utumikiwu ndipo limatikumbutsa kuti Yesu ndiye maziko olimba ndi mwala wapangodya wamphamvu za utumiki.

Kwa zaka zokwanila makumi asanu ndi awiri (70yrs) Mulungu adalilika ndi kuteteza kuthandiza ndiposo kulondoza ntchito za utumiki wa Stonecraft. Mu mumukhalidwe wosintha sinthawu, zinthu ziwili zakhala zosasunthika kuzipeleka kwathu muapemphelo ndikufalitsa uthenga wabwino.

Stonecraft mwaposachedwa yagulitsa malo amenewa ndikusuntha ku malo ena ocheperapo ama office awo kupeleka mpata wopitilirabe ndi kugwilitsa ndarama zotsatila pa ntchito yolarika ndikufalitsa uthenga wabwino.

UTSOGOLERI WAWO WA STONECROFT

Astsogoleri a Stonecraft amagawana nawo maudindo ndi kalongosoledwe ka zochitika za siku ndi siku ku maofesi aakulu ndi mmadela ena.

 
 

 

DR NAOMI CRAMER OVERTON (President ndi Bwana wamukulu)

Dr. Naomi Cramer Overton, Doctor of Intercultural Studies from Fuller Theological Seminary, researched nearly 30,000 families to develop a model to move faith communities and families to give, serve and grow in their compassion and character. She served as president and CEO of MOPS (Mothers of Preschoolers) International, she holds an MBA from UCLA and a degree related to culture, poverty, and communications from Stanford University. She is now the President and CEO of Stonecroft.

A DORIS THOMPSON - Vice President of Transformation (President wachiwili wa utumiki wofikila mmadela)

A Doris Thompson amathandiza azimayi kuyika masomphenya awo ndi maganizo awo mukuchitachita ngati wachiwiri kwa president wa utumiki wofikila mmadela iwowo a Doris zolinga zawo ndikufikila azimayi ochuluka mmadela ochuluka ndikuthekela kwa njira zonse. Amagwira ntchito kutukula mautumiki ofikila mmadela ndikukhazikitsa odzipeleka a Stonecraft kubzyala madela ena awutumiki.

Alipo azikulu akulu ena ammaudindo ndi gulu la utsogoleri amene ambiri aiwo simungayenele kulumikizana nawo

Stonecroft utumiki wawo ndiwokhumbitsitsa kukulumikizanitsani azimayi kwa wina ndi mzake ndi madera ena ndi anzake

A Stonecroft amalimbikitsa azimayi kupeza njira zothekela kupanga kulumikizana ndi azawo m'madera ndikuyitanila kumaphunziro a baibulo a mtsogolomu mudera kapena mzinda wawo

Ndi osavuta kusatawa aziphunzitsozi amadzetsa mupweya wabwino wa uzimu kwa okhulupilira akale komatso alendo ndi baibulo.

Utumiki wa Stonecroft umamva ndi kuyamikila zofunikila m'zimayi ndi Khristu, mumakhuza aliyense mudela lake , mwamuna wake, ana anzake anasi ndi ogwira naye ntchito limodzi.

BISHOP DAVID AKONDOWI - FOUNDER OF THE AFRICA TRAINING BIBLE SCHOOL, UNITED CARRIBEAN TRUST (UCT) TANZANIA REPRESENTATIVE

Ndiwoyimila ndinso ndimuyambi wa African Training Bible School (ATBS) ndiso, mbusa wankulu wa house of freedom, Tanzania komwe (UCT) anakhazikisako kutukula azimayi ndi zochitachita zosoka yemwe izakhale chiyambi chazochitika zamagawo za azimayi a

Anagawa nafe mwambi wa chintanzania. Ku Tanzania tili ndi mau otchuka kwambiri momwe tikatathauzila amamveka kuti "Phunzitsani mzimayi kuti mdera lonse mupindule"

Stonecroft timapeleka chilimbikitso ndi kuthekela kolimbitsa amayi kukhala ochita-chita pofikila madera awo.

The African Stonecroft Model will create two distinct Bible Study groups:

•  Stonecroft Bible Study Outreach Group

•  Stonecroft Bible Study Discipleship Group

Within the initial Outreach Classes new Guides will be introduced to Stonecroft and learn how to establish their own Stonecroft Bible Study Outreach Group. New believers or unbelievers will then be encouraged to join these new Outreach Groups.

Stonecroft Bible Study Discipleship Groups will be made up of women who have completed the Outreach Group 'Trinity Series' and are not ready or able to Guide but want to continue within the Discipleship Group sessions. This will enable continual growth and expansion within Stoncroft utilizing much of the other excellent Stonecroft Bible Study material to be translated into Chichewa for Malawi.

DONGOSOLO LACHIKHULUPILIRO CHA STONECROFT

•  Utumiki wa Stonecroft umakhulupilira muuzimu, wonsewofikapo kwathunthu ndi kulimbikisidwa kwa m'malembo-baibulo ndilopanda kalema ndipo ziphunzitso ndi ulamuliro wake ndizofikapo zapamwamba ndimapeto.

•  Timakhulupilira mu utatu woyera wa uzimu, Mulungu tate Mulungu mwana ndi Mulungu Mzimu woyera.

•  Timakhulupilira umunthuwa Umulungu, umunthu ndi umulungu wa (Yesu Khristu ndi Mulungu ndi Mulungu wozionetsera ku thupi) wobelekedwa ndi muzimu woyera , mulungu yese, Munthu yense umnthu wa nzimu woyera.

•  Timakhulupilira kuukitsidwa kwa yesu khristu, kuti thupi lake linaukitsidwa kwa akufa, mwamalembo, ndipo anakwela kumwamba anakhala kudzanja la manja la Mulungu ngati wotinenera zabwino okhulupilira.

•  Timakhulupilira kuchimwa kwa munthu kuti munthu yese anabadwa ndi uchimo, ndiyeso yeka mombolo ku uchimo.

•  Timakhulupilira kukuyeletsedwa, kuti Yesu anadza ngati nsembe ya ochimwa pamaso pa Mulungu, pamene anakhetsa mwazi wake ngati dipo kuuchimo wadziko lonse lapatsi.

•  Timakhulupilira kufunika kwa kubadwa mwatsopano

•  Chipulumutso ncha chisomo, kuzela muchikhulupiliro osati ntchito zabwino mu umoyo wamunthu wokhulupilira.

•  Timakhulupilira muukuwukisidwa koonekelatu kwa thupi kwa onse ochimwa ndi oyela mtima.

•  Timakhulupilira mukulalikira uthenga wabwino kudziko lapasi-chofunika chahikulu cha Mulungu ndicho kuti anthu ake mumbadwo uno alalikire uthenga wabwino kwa cholengedwa chake (Munthu) aliyense.

•  Timakhulupilira kubweleranso kwake kwachiwirikwa yesu khristu monga mwa malembo.

ZIPHUNZITSO ZAM'BAIBULO ZA STONECROFT

Takulandilani ku Stonecroft ziphunzitso zam'baibulo timapanga mau a Mulungu kufikila aliyese kwa kuwa werengera pomwe ali pa ulendo wawo wauzimu

Tikupemphela ndikuyembekekezera kuti ziphunzitso zimenezi zitsegula mwayi ochuluka kuti inu mukhale ofikapo ndikulimbikitsa kuti muliyike dera lanu kudziwa uthenga wabwino wa Yesu Khristu.

MOWUNIKILAPO

Ziphunzitso za m'baibulo za Stonecroft zinakhazikitsika maka-maka ngati njira yosatilapo pa kufikila kwa m'madera ndi misonkhano. Ziphunzitso zafikila mwakuya ndikugwilisidwa m'ndende, muzintchito, mumipngo ndi m'madera osiyana siyana.

ZOFUNIKILA ZOPENYEKA

Ziphunzitso za m'baibulo za Stonecroft amayesesa kuphatikiza kuutumiki uthenga wabwino umalukidwa kudzera muphunzitso uliwonse la baibulo la Stonecroft

Phunzilo lililonse limakonzedwa ndikuchitidwa mwakuti onse osazoloweleka ndi mau a mulungu angatenge nawo mbali zolumikizilana ku bukhu la mgwirizanowakasindikizidwe ku chipanganop chasopano za mu baibulo lomatsulidwa mu Chiswahili. Kupeleka kuphweka kwa oyamba kumene omwe sanazolowele buibulo kopeza mavesi osiyana siyana mmabukhu amu baibulo

Each study is prepared and conducted so that those unfamiliar with God's Word can participate. Unfortunately many of the women or youth taking part on the studies in Africa will not have their own Bible so page numbers have been removed from the Bible study material and a Bible Verse Handbook has been created in Chichewa with every Bible verse referenced within the Study Book, these have been done in sequential order in each lesson. Obviously if a participant has a Bible then the Bible Verse Handbook is not needed.

Ziphunzitso za mubaibulo za Stonecraft, mumakomo mmalo ogwilira tnchito , mmatchalichi mmasukulu ngakhale malo apanja mamadera la Africa.

Anazilongotsola kufikila ziphunzitso zapadela ndi mabuku am'baibulo ndipo zimapezeka m'milingo ya ongoyamba kumene nd ozama kwambiri.

Ziphunzitso za m'baibulo za Stonecraft ndizophweka kugwilitsa ntchito m'malo a magulu ang'ono-ang'ononditso mmalo akulu akulu ndipo zimapelekedwa mlingo yosiyana-siyana wamuutali wa ziphunzitso mpaka khumi ndi zinayi.

Ziphunzitso zambiri zili ndi bukhu lotsogolera lotsogoza mtsogoleri kuchititsa ziphunzitso buku lophu8nzilira limagwiritsidwa ntchito ndi wophunzila aliyense payekha.

All Stonecroft Bible studies include a Guidebook for the Guide to facilitate the study. The Study Book is used by each participant along with her Bible or Bible Verse Handbook.

Zokambilana pa gulu ndizofunika kwambiri pakuphunzila ndi kukula pamodzi.

ZOPHUNZILA ZOYENELA

Muziphunzitso za m'baibulo zambiri za Stonecroft wotenga nawo mbali amagwiritsa ntchito bukhu laophunzila ndi baibulo la Swahili Union New Tastament lopezeka ndi a Tanzania Bible Society. Olo mwina kamasulidwe kamasuloidwe kalikose kogwilizana dziko ndi dziko.

Magulu ophunzilawa nthawi zambiri amapezana kamozi pa tsabata pa mphindi zitsanu ndi kamodzi (60min) kufikila mphindi zitsanu ndi zinayi (90min) ngati nthawi ndiyochepa magulu amachiona choyenela kugawa ziphunzitso patheka zokambilana zimachokela mumayankho ogawana kumafunso ochokela m'baibulo a ziphunzitso nditso mukuwelenga kwa malembo.

Mukulitsa utumiki mumadela osiyana siyana ndi utumwi choyenela kuti Gulu liyang'ane njira zochulukitsa mwakuti enatso mumadera athandizidwe muchoonadi cha mau a Mulungu.

KUSANTHULA KWA ZIPHUNZITSO ZA BAIBULO .

Pali njira zitatu za Stonecroft ziphunzitso za mubaibulo ndizo

•  Chiyambi cha ziphunzitso

•  Ziphunzitso za okula mu ukhristu

•  Ziphunzitso zina.

Tikulimbikitsa omwe sanayambe atengapo mbali pa ziphunzitso za Stonecroft kuti ayenela kaye kuyambala ndi chiyambi cha zi[phunzitso Yesu ndi yan? Mulungu ali monga chani? Ndi nzimu woyela alikuti? Ndizoyenela kwa onse ongoyamba kumene ziphunzitso ndi onse ofuna mayankho kwa zikhulupiliro zawo ndi mafutso awo.

MFUNDO ZA STONECROFT PAZIPHUINZITSO ZA M'BAIBULO

Utumiki wa Stonecroft umakhazika mfundo paziphunzitso zake za baibulo nchofunika ndichakuti alityese amene akutenga nmawo mbali ndi Stonecloft ndi ziphunzitso zawo zam'baibulo asate mfundo izi

•  Uthenga wabwino wa Yesu Khristu womwe uli woyikidwa muziphunzitso zones zoyenela kupelekedwa momveka, mosatidwa bwino lomwe.

•  A utumiki wa Stonecroft sakhala nawo udindo pa ziphunzitso miyambo chabe ngakhale zochitika pandale kumbali kwa mfundo ya chikhulupiliro chawo.

•  Onse omwe ndi khuzidwa ndi utsogoleri wa utumiki wa Stonecroft azatsata izi:-

Azavomeleza za mfundo ya utumiki ya chikhulupiliro chawo

Azagwira ntchito moyanjana ndi mipingo yonse ya mudela mwawo

Azaonetsetsa kuti dongotsolo lomwe lapangidwa pozakambilana zokhuza moyo wa anthu ndi ndale sidikuonetsela udindo wawo ndi mbali yawo ya utumiki wa Stonecroft.

Mundondomeko ya kuphunzila naibulo kwa Stonecroft zinaganizilidwa kuti otenga mbali ogwilitsa zokhazo zobvomelezeka zida ndi Stonecroft monga bukhu lophunzilira ndi bukhu losogolera.

Muziphunzitso za pachiyambi kunaganilizidwa kuti onse akupemphedwa kumalidzitsa chofutsila chaziphunzitso za Stonecroft. Otsogolera ndi ogwirizanits amasankhidwa ndi kuphunzitsidwa ndi atsogoleri aziphunzitso za baibulo a m'madera . chioneselochi ndikuyetsela kwa a Barbados

Stonecroft ziphunzitso za m'baibulo azimayi kuphunzitsa otsogolera omwe azafikitse ziphunzitso za baibulo za Stonecroft mu Tanzania, Malawi, Uganda ndi mayikom ena mu Africa.

NDONDOMEKO YA KUPHUNZILA OLONDOLERA ZOMUYENELEZA OLONDORELA

Zofunikila za olondolera ndi kusogolera ndi kulondolera ziphunzitso zabaibulo.

Pomwe olondolera akugwira nthchitoyi ali ndi mwayi otensela dera lawo poyambitsa kuti enatso akhale ndi chiyanjano chawo ndi Yesu Khristu

WOLONDOLERA ZIPHUNZITSOZAM'BAIBULO WA STONECROFT

•  Amapemphelera nthawi ndi nthawi yemwe akhale muziphunzitso za baibulo

•  Amayamba ziphunzitso za Baibulo ndi pemhero

•  Otsogolera baibulo wa Stonecroft amaphunzitsidwa ndi otsogoza kukhazikitsa ziphunzitso za baibulo amakhala woziwitsidwa ndikukhonzelekesedwa munjila zopititsa patsogolo la luntha lake ngati wolondorera ndi mtsogoleri wake.

•  Wolondolera amatsatila mfundo zones za Stonecroft kuphunzitsa baibulo ndipo oyenela kuziwisa otenga mbali momwe angayenele kukhala ochita ndi umozi pagulu posatila zotsogoleza zomwe zayikidwa muchiwonetselo ichi.

•  Amakhozeketsa gulu lake kuyang'ana maso pamafutso a ziphunzitso zabaibulo

•  Amapeleka mwayi kwa ophunzila ndi kutenga mbali kuti aziwe za momwe uliri utumiki wa Stonecroft ndikuwuziwitsa kwa otenga mbali mderaro za mwayi oti iwo angalumikizane ndi amdera lina.

•  Amayetsesa kufuna kuwalondolera otenga nawo mbali kupeza kupeza mayankho kwa malutso azikhulupiliro zawo

•  Zokambilanazo zimalimbikitsidwa p-okhapo pomwe baibulo limanena osati kuyima pamene mpingo ndi zikhulupiliro zawo zimaphunzitsa.

•  Amafunitsa kusayang'ana zomutsokoneza nditso kumutalikitsa kuzinthu zochokela ku zomwe ziphunzitso, zochitika mmadera lamuzabndale ndi zina zomwe anthu kapena mipingo amakangana.

WOLONDOLERA AKHALE NDI IZI:-

•  Wolondolera akhale ndi chiyanjano ndi Yesu Khristu

•  Akhale ndi chikhumbo chofuna mphavuyo sintha moyo yam au a mulungu

•  Akhale wogwizana ndi mfundo ndi ndondomeko za ziphunzitso za baibulo za Stonecroft

•  Amatolerana ndi kugwila bwino ntchito ndi anthu ena.

•  Ali ndi chifuniro chotengela anthuena kuziwa mau amulungu ndi kuwakulitsa muuzimu ngati akhristu.

KUSANKHA OLONDOLERA WOYENERA WAZIPHUNZITSO ZA BAIBULO

KASANKHIDWE KA OLONDOLERA

In Africa, unless the Pastors catch the vision it is very difficult to introduce the programme into the churches, schools or orphanages associated with these churches. So we have identified Pastors from throughout Africa. These Pastors in Africa are part of the Africa Training Bible School and will be trained to be Guides, they will then train their key women within their local church.

Makamaka azibutsa omwe amaphunzitsidwa kukhala olondolera angapeze ena muderalo moganizila, mwapemphelo ndi dongotsolo, kusankha athu oyenela ngati olondolera mudera lawo ndipo kupeleka mwayi wakukula mochuluka wa ziphunzitso zamubaibulo za Stonecroft

Nchoyenela kuyang'ana zoyeneleza wolondolera yemwe angasatev bwino malo ofunikila poganizila anthu otumikila ngati olondolera

•  Kupemphera pasanafike tsiku la ntsonkhano lokumanira ndi ofunawo kupempha mulungu kupeleka mzeru kwa inu ndi ofunawo ndinso Mzimu wa chiziwitso mogwilizana ndi udindowo.

•  Kupeza nthawi yoziwana bwino lomwe muyenela kuziiwitsa za ziphunzitso za baibulo za Stonecroft ndi utumiki wake ngati nkoyenera

•  Muyang'anile mwamasdera munthawi yazitsankho omwe ali mkati mwa folamu yofutsila yaziphunzitso za Stonecroft.

•  Pelekani chiziwitso pa utumiki wa Stonecroft muwayang'anize ofuna kukhala wotondolera ku :-

•  Ziphunzitso za Stonecroft bukhu la banja

•  Fikani mu stonecroft corporate pa internet yawo stonecroft@org kuti muziwe zambiri

•  Mufutse olondolera kuti anene mwatsatane tsatane momwe anakhulupilira Yesu Khristu payekha pa chipulumutso chake ndipo apelike mavesi a m'baibulo omwe akusimikiza kuti za ukadaulo pa chikhulupiliro chake.

•  Mufuse olondolayo kufotiokoza satane satane m'mene angayankhile za mbiri yokuza Yesu Khrisu

•  Muziwepo kwa olondolerawo chomwe chinawakopa kugwira ntchito ndi Stonecroft mziphunzitso a baibulo.

•  Muyang'ane kufunitsisa kwawo ogwila ntchito ndi zikhulupiliro zikhalidwe ndi zipembezo zosiyana-siyana.

•  Muwafuse olondolerawo zina zimene iye amachita ndiukadaulo wake potsogoza ziphunzitso za baibulo

•  Muwonesese ndiwoziwitsisa mfundo za Stonecroft muziphunzilo za baibulo ndi dongotsolo la chikhulupiliro chawo.

•  Oyenela kukulondolera ayenela kuwerenga ndikumvetsa mfundo za Stonecroft pakusasokonezeka.

ZOFUNIKILA ABUSA KAPENA NGWILIZANITSI

•  Alandile folam yakutha yofunsila kuchokela kwa woyenera kulondolera

•  Alondole moyenela mkuwerenga folum yofunsila kuti atenge chitsimikizo choti umboni wa wolondolera ndi omveka bwino.

•  Mwapephero muyenela kumufutsa mafutso angapo wokhuza chiyanjano chake ndi Yesu Hhristu mwana wa Mlungu monga:-

•  Ndikufuna kuzwa za ulendo wako ndi mulungu, Khristu kodi wagwilapo gawo lanji?

•  Ngati wotenga mbali pa ziphunzitso za baibulio za Srtonecroft atakufutsa zamomwe ungakhalire pa chiyanjano ndi Mulungu inu mungamuyankhe motani?

•  Mukuwumvetsa bwanji uthenga wabwino, ndipo mungaulumikizitse motani

•  Mungathe guganizila kuwerengapo mabuku la Mungathe kuchikhulupila? Ndi olondolerayo.

•  Funani nthawi yolumikizana ndiolondolerayo gwilitsani tchito zida izi

•  Bukhu lamanja la African Stonecroft ziphunzitso za m'baibulo.

•  Ndondomeko polondolera patsogolo pa bukhu la la dongotsolo ngati sanayambe achitapo phunzilo la Stonecroft muyenela kugwila ntchito limozi muziphunzitso zochepelapo mukabuku ka Yesu ndi ndani? Kuti amvese zomwe zili nkati.

Abutsa kapena olumikizitsa asunge chikalata chofunsila mumabukhu awo.

Kumbukani kuti sionse ali wokonzeka kukhala wolondolera ngati mwaziwisana kuti wian wake Sali woyenera kukhala wolondolera posasata masomphenya eni eni a zophunzitsa m'baibulo za Stonecroft mupewe zokangana za kuthupi pena zandale mungomutengera mwabwino kumusiyitsa kulondolera mwa njira ina mumutenge kukhala mmodzi wotenga nawo mbali ya kuphunzila nawo ziphunzitso za Baibulo, muyenela kukambilana izi ndi mtsogoleri wankulu kapena m'butsa wake.

Mukamaliza ntchito yophunzitsa wolondolerawo mulumikizane ndi mulangizi wankulu pa makina a intanet kwa African Stonecroft wamdela lanulo kuti mutengetso ndondomeko ina yolondola

Wamkulu wamuderalanulo azalumikizana ndi a stonecroft utumiki wothandiza waku America pa mfundoyi atha kupanga zimenezi polemba pamakina a internet ku Connections @stoncroft.org

Chone musayiwale za olondolera address yake ndi nambala ya lamya nditso addrees yapamakina a internrt monga momwe mwatiwonela pankhani ya ndondomeko ya kaphunzitsidwe ka Baibulo

Pomwe a Stonecroft azalandile uthengawu osankhidwa watsopano wolondolerayo azalandila pamakina a internet kulandilidwa jkwake komwe kuzatanthauzidwile mchilankhulo cha kudera lakelo kumuziwitsa za udindo wake watsopanowo , olondolera azakhalatso gawo lamulumikizano wa odzipeleka ndipo athatso kulandila nyuzi pepala ya Stonecroft ya chingerezindikuthekelatso kulu ndi atsogoleri pa makina a internet zokhuzana ndi utumiki wa Stonecroft.

Kudziwitsa za olondolerawo kutha kusimikidzila za kuziwika kwawo ngbati atsogoleri, timamuyika munthu aliyense wokhunzika muutumiki wofunikila kwambiri ndipo ngati mbali yofikilitsa ziko lathu kwa Yesu Khristu.

KUSULA BWINO WOLONDOLERA WA STONECROFT

Wolondolera wophunzitsidwa bwino ndiwofunikila kwambili paukafdaulo wa anthu okumba chikhulupiliro nditso omwe akhala muziphunzitso za baibulo kwa zaka zambiri.

Agwirizanitsi ambiri amalemba ma nyuzi pepala kwa nthawi ndi nthawipofuna kulumikizana nawo, mikumano yoitanitsa, ngati ili yopezeka pa SKYPE, olo njira zina zamakina a internet ndikuthekela kwina kofuna kolumumikizana ndi olondolera a mdela lanu.

Agwirizanitsi ayenera kupanga ndiondomeko pa kanthawi pachaka yoti kulumikizana ndi olondolera powayamikira mowathandizila ndi chilimbikitso ngakhale kuwakhazikitsa momwe angayendetsele bwinon ziphunzitso zamubaibulo za Stonecroft.

Zambiri zimachitika zothandiza kuleza mkulumikizana, pemphero, kugawana zofuna zanu ndinso kuphunzira luso lina, ndikudziwa momwe angayankhile mafunso ovuta

Nthawi yophunzitsa olondolera itha kukonzedwa pachaka ngati pokumana kwa Khirisimisi olo mwina zosangalatso ngati tsiku lokumbukira kubadwa mwinanso tchuti kumene chapadera.

Izi ndi zina zoganizilapo pakasankhidwe ka nthawi yophunzitsira olondolera

•  Nthawi yapadela ya mapemphero ndi chiyanjano

•  Nthawi yopikkisana za malembo, pemphero lapadela lodzipeleka, poyamika ndikulimbikitsa olondolera potumikila.

•  Pokhazikita olondolera ena ndipogawana zotsatila zabwino pamaphunziro awo

Ntawi yabwino ngati ugawidwe wa umboni, kuchulukitsa utumiki mdera lanu, kukhazikitsa utumiki wa Stonecroft kwa mpingio mdela lanu olo bungwe lochita chita mdera lanulo. Iyi itha kukhalanso nthawi yophunzira kwa wina ndi mzake. Mulore olondolera agawane momwe amaitanila otenga nawo mbali, nthawi yobvuta yomwe akumana nayo, ndi pomwe amuona Mulungu akuchita ntchto yyake mwa otenga nawo mbali (m'moyo wawo).

Mumalize nd chilimbikitso ndikupemphelerana wina ndi mzake

NDONDOMEKO YOLONDOLERA

CHOLINGA:

Kufikira mdera: ziphunzitso zimapeleka njira yabwino yogawana chipulumutso ndi ena mwa Yesu Khrisu.

Tikuyang'ana zopititsa patsogoloziphunzitso za mubabaibulo kudzera mu mipingo kuyambira mu African Bible Training School (ABTS) KU Tanzania Malawi ndi Zambia ngakhalenso Hope Community Centre, Kampala, Uganda.

The Pastor will identify a Church Guide, trained to lead a Bible Study group, who will start by going through the Stonecroft Bible Study Outreach Trinity Series starting with 'What is God Like? then 'Who is Jesus' and lastly "Where is the Holy Spirit?"

On completing the Trinity Series they will be encouraged to become Guides, using this Handbook enabling will enable them to start a Stonecroft Bible Study Outreach Group in their homes or local communities.

Pomaliza azalimbikitsidwa pokhala olondolera, pogwiritsa ntchito chionetsero cha ophunzira a mu Africa ngati mbali yao ya chiphunzitso, ngakhalenso bukhu limeneli, kuwapatsa mwayi woyambitsa phunziro la mubaibulo mmadera awo akamabwelera mmamidzi mwao, poitanitsa anzawo, mabanja, ogwira nawo ntchito ndi anansi awo.

Utumiki . A khristu atsopano ndi okhwima monga azibutsa pa (ATBS)atja kuphunzira zambiri za mulungu ndikukula mu chiyanjano ndi Iye. Ziphunzitso zimafotokozera za momwe tingaikile mfundo za mbaibulo m'moyo wathu wa tsiku ndi tsiku.

UPADERA

Ndiye chomwe chimapangitsa ziphunzitso za mu baibulo za Stonecroft kusiyana ndi ziphunzitso zina zopezeka pa msika nchiyni?

•  The studies are designed to be used with a New Testament however the page numbers have been removed in the Chichewi translation of the Bible Study and a Bible Verse Handbook has been created in cases where the participants do not have a Bible of their own.

•  Ziphunzitso zimapangidwa ntchito chipangano chatsopano chomwe chili chopezekelatu kudzera ku bungwe la ma baibulo la Tanzania, cholinga chawo ndikufalitsa uthenga wabwino wa Yesu Khristu ndikulimbikitsa malembo kwa anthu m'moyo wawo wa tsiku ndi tsiku bukhu la mgwirizano wa tsopano mchilankhulo cha chiswahili ndilopezeka ku bungwe la ma baibulo lopezeka mkati mwa Tanzania mdera la Dodoma. Masamba ena atanthauzilidwa mu chiswahili chophunzitsa baibulo kugwirizana ndi Kamasulidwe ka umodzi (union verson)

•  Ziphunzitso zalembedwa mwandondomeko yotsatidwa bwino kwa omwwe ndi oyamba kumene kuphunzira baibulo.

•  Kumbukirani kuti ndondomeko yolondolera baibulo simphunzitsi koma ndikuphunzira limodzi ndi omwe akuchita nawoziphunzitso za baibulo.

NDONDOMEKO ZABWINO

Ziphunzijtso za baibulo za Stonecroft sizobvuta kuwenga

Zoyenera kudziwa olondolera zoikida mmadontho a malire a bukhu lolondolera. Izi nzoyenera kuwerengedwa mokwweza kwa onse otenga nawo gawo.

Madontho angapo (....) akusonyeza kuti olondolera ayenela kulola gulu kutenga nawo mbali poyankha mafunso, kuwerenga nawo vesi la mu baibulo mwina kueleka mfundo pa mutu omwe ukukambidwawo.

Zilembo zotsindikizidwa mowonjezera ndikusonyezedwa mu baibulo motsatana ndi madontho asanu zikuwonjeza vesi lomwe liyenera kuwerengedwa mokweza pa nthawi ya ziphunzitso ndi mmodi wagululo.

Ngati mosonyezera zili motsindikizidwa mwanthawi zones, zikusonyeza kuti nzotalikitsidwa kwambiri kuziwernga pagulu kapena sizofuna kupeza yankho lake.

NTHAWI YOYANDIKIRA ZIPHUNZITSO ZA BAIBULO.

Zofunikira zina zochepa:

Uyenera kubvomelezedwa ngati wolondolera wa Stonecroft momaliza folomu yofunsira ya ziphunzitso za Baibulo za Stonecroft yomwe yatanthauzilidwa muchilankhulo cha chiswahili kwa ofunsila a Tanzania.

Tikufuna kudziwa udindo wanu ndi mbali yanu pa mpingo.

Tikufuna kudziwa ngati mwawerenga mfund za zautumiki wa Stonecroft ndi mfundo yachikhulupiliro kuti palibe chomwe mwakhuzidwa nacho

ZOFUNIKIRA PA ZIPHUNZITSO

•  Bukhu la chiyambi utatu woyera lophunzilira lotanthauzilliqwa mu chiswahiri litha kupezeka kuchoka ku likulu la (ATBS) Mbeya, Tanzania.

•  Mabukhu ophunzilira atha kutengedwa kuchoka ku Mbeya, Tanzania.

•  Baibulo la chiswahiri mgwirizano litha kupezeka kuchoka ku bungwe la mabaibulo la Tanzania.

•  Kodi mungazikhulyupilire izi? Latanthauzilidwa mu chiswahili ndipo litha kupezeka ku likulu lawo la (ATBS) ku Mbeya, Tanzania.

•  Makhadi a chidziwitso atanthauzilidwanso ndipo atha kupezeka ku likulu lawo la (ATBS) ku Mbeya, Tanzania.

•  Fomu ya wolumikiza (wolondolera) lofunsira za uphunzitsi wa baibulo titha kupezeka ku likulu la (ATBS) ku Mbeya, Tanzania.

Mupeze mala oyenelera a ziphunzitso zamubaibulo, muganizile zohita maphunziro mnyumba, tchalitchi, mkalasi pa tsiku loweluka, mwina panja pa mthunzi wabwino pansi pa mtengo.

KUKHONZEKERA ZIPHUNZITSO

Mumalizitse ziphunzitso polemba mayankho mu bukhu lophunzitsira musanawerenge bukhu la ndondomeko. Izi zikuthandizani kumvetsetsa malingaliro omwe ena atadutsemo kukafikira mayankho oyenelera

Muphunzire kuwerenga ziphunsitso mokweza ngati kungakhale koyenelera. Musindikize malembo ofunikira ndi mau ena apadera omwe angakuthandizeni kumvetsa bwino lanu kugulu.

Under normal circumstances lessons should not exceed 1 - 1 1/2 hours particularly if the Bible Study is part of the Africa Women's Empowerment Program (AWEP) because the ladies will have to leave and start their Vocational Training Lessons.

At the same time as AWEP students are enjoying their Bible Study their child will be attending their PowerClub to be trained in the ways of God through Africa Bureau of Children's Discipleship Curriculum including the Grow and Go curriculum alongside the Drop of Hope Organic Kitchen Garden project as well as the 'Kids in Ministry International' curriculum and other children's ministry including Kids Evangelism and Youth Discipleship Programs.

Initially the locations will be:

Tanzania - Africa Training Bible School (ATBS) - Mbeya Tanzania (Swahili)

Uganda - Hope Community Centre, Kampala (English)

Malawi - Africa Training Bible School (ATBS) - Uluwa and Vulwa, Malawi (Chichewi)

DR Congo - Africa Training Bible School (ATBS) (French)

NTHAWI YA ZIPHUNZITSO

Nthawi zonse yambani maphunziro ndi pemphero, ngati wina wake wanena pempher, muganizile kuti gulu lilembe pa zopemphelerapo pa tsamba la bukhu lophunzilira kumapeto ngati chikumbutso kudzapemphelerapo mkati mwa sabata.

Ngati pempho ndilofunika msanga, muziikepo kuyamba kwa ziphunzitso mupemphero lotsegulira.

Mukumbukire kuti pachiyambi pa phunziro la gawo lirilonse monga yesu ndiye ndani? Munthu yense ayenera kulemba mayankho ake mubukhu lophunzilira pa phunziro loyambilira. Pazotsatira zina zophunzilira mulimbikitse gulu kumaliza maphunziro pakuyamba kwakukumanako potsindikiza mayankho mubukhu lophunzilira musanafike kukalasi.

Muerenge ndikupeleka uthenga mubukhu lolondoza ndondomeko mwapamwamba moyang'ana maso bwino lomwe kwa ophunzira. Wolondolera akuphunzira nawo limodzi ndi gulu kuli oyenera kukhala kadaulo pa baibulo.

Wolondolola amayi kumveka bwino ndi mulingo wa ziphunzitso potsatira izi:-

•  Kuyamba ndikutsinzina panthawi yake, kumbukirani zambiri za ziphunzitso zizikhala zophatikizana ndi ndondomeko ya amayi kupatsidwa mphamvu ya Sstonecroft, ndiye, azimayi ayenera kuchoka ndikupita kuziphunzitso zantchito yamanja pamapeto pake.

•  Gwiritsani ntchito bukhu lolondoza ndondomeko ndi baibulo lwa chiswahiri mgwirizano ndi ena mwa ma baibulo oyenera omasulidwa bwino ku maiko ena, sipafunikanso zipangizo zina za padera..

•  Limbikitsani wina aliyense kutenga nawo mbali muzokambirana, kusalora kuti wina akulamulira kwambiri, muyenera kukhala okoma mtimapomwe mukulibikitsa ena kutenga nawo mbali posamukhumudwitsa yemwe akutenga nawo mmbali kwambiri.

Muyike maso pakuphunzira za yesu, osati osati ziphunzitso zawamba, za ndale kapena zochitika mdera, mafunso aziphunzitso za wamba amatha kutengedwa bwino panthawi inayoyenera bwino.

Nthawi zones yang'anani omwe ali mgulu omwe angadzakhale olondolera ziphunzitso za mtsogjolo.

Ngati wolondolera mukhale chitsanzo choawonetsa tsankho. Muletse anthu kuleka kukambirana zinthu zimene siziyenera kukambidwa pa gulupo monga mikangano ya kunyumba kuwonjezera pa zochit za pa gulupo. Mupemphere ndi anthuwo ndikuwalimbikitsa kufuna chitsogozo cha Mulungu.

Pomaliza pa dondosolo la azimayi kulandira mphamvu a Stonecraft, aliyense amene angachite kulondolera bwino asankhidwe ndikuphunzitsidwa kupeleka mwayi kwa omwe amaliza maphunziro kubwelera kumanyumba kwawo potenganso ndi ziphunzitso zawo kumadera kwawoko.

Mufunse otenga nawo mbali za omwe angawaitane kumaphunziro ena baibulo. Muwalimbikitse kupemphelerana mayina wina ndi mzake.

ZOYENERA KUDZIWA (OSAIWALA)

•  Ngati muli olephera kuwerenga maphunziro a baibulo pazifukwa zina, wina obvomelezeka kapena wophunzira bwino wapambali ayitanidwe kutenga malo anu.

•  Simuli ololedwa kupeloeka bukhu la ndondomeko yolondolera kwa membala wina wa mkalasi lanu.

AFRICA NDONDOMEKO YA AZIMAYI KUPATSIDWA MPHAMVU (ANZKM)

Dongosolo limeneli lakaphunzitsidwe ka baibulo ndilokhonzedwa kugwira ntch ito limodzi ndi azimai kupatsidwa mphamvu

Ku UCT timakhulupilra kuti amayi kufikira ku maphunziro, utsogoleri wophunzitsidwa bwino, zitha kusintha dela lawo ndinso dziko lonse.

Azimayi a dongosolo Kupatsidwa Mphamvu amalembedwa kwa chaka chimodzi.

Mwezi uliwonse amayenelezedwa kuchita nawo ziphunzitso za sabata zokumana ndi Mulungu mu nthawi ya pemphero, "kutengera mwai zipangizo za ziphunzitso za baibulo za Stonecraft.

Ayeneranso kuchita nawo maphunziro osiyanasiyana opatsidwa mphamvu ngati kupanga ma diresi ndi luso, ndikuphunzira luso la kompyuta ndi zina zotere.

Koma koposa zonsezimathandizira kuts egula zitseko za mwayi woti adziwike ndi Stonecraft, ziphunzitso za baibulo ndi zipangizo za utsogoleri.

Ndiwoyenerezedwanso mwana mmodzi pa nthawi kuchita nawo dongosolo la madyedwe apakalabu kuti azidyetsedwa ku thupi ndinso ku uzimu.

Ndi khumbo UCT' s kuti azimayi ku Tanzania, Uganda, Malawi munjira yomwe imawonetsera chikondi cha Mulungu pomwenso akupatsiwa mphamvu kudzipulumutsa okha ndikudyetsedwanso mu uzimu wao.

CHITSANZO CHABWINO CHA UTUMIKI WACHI AFRIKA

Utumwi wachitsanzo wachifilika watsimikiza kuti nkwabwino kugawa kuti muchulukitse ndinso kuchulukitsa nkwabwino kuposa kuonjezeera

1. Chitsanzochi chamu Africa chiidzayambitsidwa kaye poyamba mu Tanzania kudzera ku (ATBS) cholinga chake chenicheni ndikuphunzitsa a Stonecraft ziphunzitso za mu baibulo kwa olondolera. Pogwiritsa ntchito kanema wa ziphunzitso ndinso bukhu la olondolera lamanja la ziphunzitso, tidzapatsa chitysogozo kwa azibusa omwe akupanga nawo maphunziro awo tsopanowa pa (ATBS) ku Tanzania komanso Malawi ndi Zambia. Azibusa amenewa adzakhala oondolera oyamba mu Tanzania Mulungu akalolra. Adzapatsidwa aliyense limodzi mwa ma baibulo la mgwirizano swahiri chipangano chatsopano, limodzi la bukhu lawolondolera ndi ndongosolo lakle ndi mabaibulo a ziphunzitso zowelenga mu ndime ya utatu woyera, mkamaka khumi a Yesu ndiye ndani? Kenako khumi a Mulungu ali ngati chiyani? Ndilotsiriza lake la kodi Mzimu woyera ali kuti? Khumi nawo.

2. Azibusa adzaqtengera uthengau ku mipingo yawo kumadela kwawoko ndikupeza mzimayi wachangu pa ntchito ya mulungu kaya ndimtsogoleri wa azimayi, pogwiritsa ntchito kanema yophunzitsirayo ndi bukhu la wolondolera la Stonecroft mu Africa la mmanja, adzaphunzitsa olondolera m'mipingo wamba yoyambira kwawoko, ndiye m'usayo mgwirizanitsi woyang'anira mayiyo

3. Wolondoler watsopano adzapatsidwa mabaibulo atsopano khumi achipangano chatsopano, bukhu la wolondolera mwadongosolo la Stonecraft, ndi khumi la mabukhu ophunzira baibulo a Stonecraft a kodi Yesu ndi ndani? Onse otanthauzilidwa mu chiphunzitso cha kwawo chomwe ndipo, adzafuna amayi asanu a mum'pingo momwemo oyenera kulondolera bwino kuti ayambe kutenga gawo. Mmodzi mwa amayi olondolera osankhidwawoatha kubweretsa mzawo m'modzi, makamaka opemphera naye ku gulu laziphunzitso za baibulo, ngati ziphunzitso za baibulo zatha adzaphunzitsa azimayi asanu osankhidwawo kuti akhale gawo achitatu la wolondolera a Stonecraft mogwiritsa ntchito kanema wophunzitsilayo ndimabukhu ophunzitsilayo ndi mabukhu ophunzilira ophunzilira baibulo a Stonecroft a m'manja

4. Adzakhala mgwirizanitsi kuwonelera olondolera asanuwo

5. M'usa adzakhala mgwirizanitsi wankulu woonelera ntchitozo.

6. M'modzi wa olondolera asanuwo pamodzi ndi anzawo opemphera nawowo adzapeza muntu wachangu m'modzi kuchoka pa mpingo wawo mwina mdelaro ndi winanso woyenera woti atha kulondolera bwino kuchoka ku mpingo wina mopmvana ndi abusa ake kumuloleza.

7. Pamodzi amayi anayiwa adzalimbikitsa anthu omwe Sali okhulupilira kulowa mgulu ophunzira atsopanowa anthu awiri aliyense. Kumbukani maphunziro a baibulowa ayenenera kusapitilira anthu okwana khumi.

8. Ngati ziphunzitso za baibulo za Yesu ndiye ndani? Zatheka ayenera kuphunzitsa amayi awiriwo (m'modzi wochoka kumpingo wake winayo ku mpingo wina) kuti adzakhale gulu lachinayi la wolondolera a Stonecroft. Wopemphera naye mzakeyo adzakhala naye kuphunzitsa mkalasi kuphunszitsa ziphunzitso zina za baibulo za muphunziro la utatu woyera.

9. Dongosololi limatsatidwanso ku mipingo ina yomwe yaikidwa nawo mu ndondomeko imeneyi

10. Ngati pali mafunso ena onse amene olondolera sangathe kuyankha ayenela kuwapeleka kwa mgwirizanitsi amene ayenera kukhal mbusa.

11. Pomwe nthawi ikupita agwirizanitsi ena adzakhala akuphunzitsa ngati mgwirizano ukukula kanema adzakhala akugwiritsidwa ntchito kwa ziphunzitso za wogwirizanitsa

12. Kumbukirani kugawa kugawa kuti muchulukitse.

13. Kuchulukitsa nkwabwino kuposa kuwonjezera

"muyenera kukhala a tcheru, kuima njii mu chikhulupiliro, khalani olimbika, amphamvu. Muchite ntchito zanu zones mucikondi"

1 Akorinte 16:13-14

 

 
 
Copyright ©  2023 www.UnitedCaribbean.com. All rights reserved. Disclaimer Click to Contact us