Project Hope     home >>stonecroft>> ziphunzitso zambaibulo za stonecroft >>mfundo za stonecroft paziphuinzitso za m'baibulo
MFUNDO ZA STONECROFT PAZIPHUINZITSO ZA M’BAIBULO
Women's Empowerment Program
Sports Bible Club
Living Water Bible Club

MFUNDO ZA STONECROFT PAZIPHUINZITSO ZA M’BAIBULO

Utumiki wa Stonecroft umakhazika mfundo paziphunzitso zake za baibulo nchofunika ndichakuti alityese amene akutenga nmawo mbali ndi Stonecloft ndi ziphunzitso zawo zam’baibulo asate mfundo izi
• Uthenga wabwino wa Yesu Khristu womwe uli woyikidwa muziphunzitso zones zoyenela kupelekedwa momveka, mosatidwa bwino lomwe.
• A utumiki wa Stonecroft sakhala nawo udindo pa ziphunzitso miyambo chabe ngakhale zochitika pandale kumbali kwa mfundo ya chikhulupiliro chawo.
• Onse omwe ndi khuzidwa ndi utsogoleri wa utumiki wa Stonecroft azatsata izi:-

Azavomeleza za mfundo ya utumiki ya chikhulupiliro chawo

Azagwira ntchito moyanjana ndi mipingo yonse ya mudela mwawo

Azaonetsetsa kuti dongotsolo lomwe lapangidwa pozakambilana zokhuza moyo wa anthu ndi ndale sidikuonetsela udindo wawo ndi mbali yawo ya utumiki wa Stonecroft.

Mundondomeko ya kuphunzila naibulo kwa Stonecroft zinaganizilidwa kuti otenga mbali ogwilitsa zokhazo zobvomelezeka zida ndi Stonecroft monga bukhu lophunzilira ndi bukhu losogolera.

Muziphunzitso za pachiyambi kunaganilizidwa kuti onse akupemphedwa kumalidzitsa chofutsila chaziphunzitso za Stonecroft. Otsogolera ndi ogwirizanits amasankhidwa ndi kuphunzitsidwa ndi atsogoleri aziphunzitso za baibulo a m’madera . chioneselochi ndikuyetsela kwa a Barbados

Stonecroft ziphunzitso za m’baibulo azimayi kuphunzitsa otsogolera omwe azafikitse ziphunzitso za baibulo za Stonecroft mu Tanzania, Malawi, Uganda ndi mayikom ena mu Africa.

Mayendedwe a Otsogolera

 
 

 

 
 
Copyright ©  2023 www.UnitedCaribbean.com. All rights reserved. Disclaimer Click to Contact us