Project Hope     home >>stonecroft>> mulungu ali ngati chiyani? - buku lothandiz
MULUNGU ALI NGATI CHIYANI? - Buku Lothandiz
Women's Empowerment Program
Sports Bible Club
Living Water Bible Club

MULUNGU ALI NGATI CHIYANI?

Buku Lothandiza

Utumiki wa Stonecroft?

Azimayi kulumikizana ndi Mulungu, azimayi anzawo komanso anthu amdera lawo.
Kwa zaka pafupifupi 75, utumiki wa Stonecroft wakhala ukudziwitsa azimayi amisinkhu yosiyanasiyana komanso amawonekedwe osiyanasiyana za Ambuye Yesu ndikuwaphunzitsa kulalikira uthenga wake wabwino.

Kufikira mzimayi m’modzi ndiye kuti mwafikira aliyense amene amadziwana naye. Kaya ndi achibale, anzake, okhala nawo dera limodzi komanso ogwira nawo ntchito, mumawafikira. Choonadi chenichenicheni cha Uthenga Wabwino chimadzetsa chiwombolo chenicheni ku miyoyo.

Zipangizo zosinthira miyoyo, kuzamitsa chikhulupiliro m’madera osiyanasiyana ndi monga:

MULUNGU ALI NGATI CHIYANI?
Mumaganiza chiyani za Mulungu?
Kodi ndi wa Ulamuliro wa mphamvu chabe
Kodi anangotilenga ndi kutisiya tokha?
Tikakhala kakasi, Iye amakhala kuti?
Dziwani chimene Baibulo limanena za Mulungu.
Tingamudziwe bwanji ngati
Mulungu osintha nyengo?
.
Stonecroft ndi utumiki wa Chikhristu wa mipingo yosiyasiyana. Umawona za ntchito zosiyasiyana, zipangizo zophunzilira komanso kuphunzitsira. Utumikiwu umalumikizitsa azimayi ndi Mulungu kuwalumikizitsanso ndi azimayi anzawo komanso kukonza ubale wa azimayiwa ndi anthu akudera kumene amakhala

 
 

 

 
 
Copyright ©  2023 www.UnitedCaribbean.com. All rights reserved. Disclaimer Click to Contact us