Project Hope     home >>stonecroft>>zofunikila >> ndondomeko yolondolera
NDONDOMEKO YOLONDOLERA
Women's Empowerment Program
Sports Bible Club
Living Water Bible Club

NDONDOMEKO YOLONDOLERA

CHOLINGA:
Kufikira mdera:ziphunzitso zimapeleka njira yabwino yogawana chipulumutso ndi ena mwa Yesu Khrisu.

Tikuyang’ana zopititsa patsogoloziphunzitso za mubabaibulo kudzera mu mipingo kuyambira mu African Bible Training School (ABTS) KU Tanzania Malawi ndi Zambia ngakhalenso Hope Community Centre, Kampala, Uganda.

The Pastor will identify a Church Guide, trained to lead a Bible Study group, who will start by going through the Stonecroft Bible Study Outreach Trinity Series starting with ‘What is God Like? then ‘Who is Jesus’ and lastly “Where is the Holy Spirit?”
On completing the Trinity Series they will be encouraged to become Guides, using this Handbook enabling will enable them to start a Stonecroft Bible Study Outreach Group in their homes or local communities.

Pomaliza azalimbikitsidwa pokhala olondolera, pogwiritsa ntchito chionetsero cha ophunzira a mu Africa ngati mbali yao ya chiphunzitso, ngakhalenso bukhu limeneli, kuwapatsa mwayi woyambitsa phunziro la mubaibulo mmadera awo akamabwelera mmamidzi mwao, poitanitsa anzawo, mabanja, ogwira nawo ntchito ndi anansi awo.

Utumiki. A khristu atsopano ndi okhwima monga azibutsa pa (ATBS)atja kuphunzira zambiri za mulungu ndikukula mu chiyanjano ndi Iye. Ziphunzitso zimafotokozera za momwe tingaikile mfundo za mbaibulo m’moyo wathu wa tsiku ndi tsiku.

UPADERA

Ndiye chomwe chimapangitsa ziphunzitso za mu baibulo za Stonecroft kusiyana ndi ziphunzitso zina zopezeka pa msika nchiyni?
The studies are designed to be used with a New Testament however the page numbers have been removed in the Chichewi translation of the Bible Study and a Bible Verse Handbook has been created in cases where the participants do not have a Bible of their own.
• Ziphunzitso zimapangidwa ntchito chipangano chatsopano chomwe chili chopezekelatu kudzera ku bungwe la ma baibulo la Tanzania, cholinga chawo ndikufalitsa uthenga wabwino wa Yesu Khristu ndikulimbikitsa malembo kwa anthu m’moyo wawo wa tsiku ndi tsiku bukhu la mgwirizano wa tsopano mchilankhulo cha chiswahili ndilopezeka ku bungwe la ma baibulo lopezeka mkati mwa Tanzania mdera la Dodoma. Masamba ena atanthauzilidwa mu chiswahili chophunzitsa baibulo kugwirizana ndi Kamasulidwe ka umodzi (union verson)
• Ziphunzitso zalembedwa mwandondomeko yotsatidwa bwino kwa omwwe ndi oyamba kumene kuphunzira baibulo.
• Kumbukirani kuti ndondomeko yolondolera baibulo simphunzitsi koma ndikuphunzira limodzi ndi omwe akuchita nawoziphunzitso za baibulo.

NDONDOMEKO ZABWINO

Ziphunzijtso za baibulo za Stonecroft sizobvuta kuwenga

Zoyenera kudziwa olondolera zoikida mmadontho a malire a bukhu lolondolera. Izi nzoyenera kuwerengedwa mokwweza kwa onse otenga nawo gawo.

Madontho angapo (……….) akusonyeza kuti olondolera ayenela kulola gulu kutenga nawo mbali poyankha mafunso, kuwerenga nawo vesi la mu baibulo mwina kueleka mfundo pa mutu omwe ukukambidwawo.

Zilembo zotsindikizidwa mowonjezera ndikusonyezedwa mu baibulo motsatana ndi madontho asanu zikuwonjeza vesi lomwe liyenera kuwerengedwa mokweza pa nthawi ya ziphunzitso ndi mmodi wagululo.

Ngati mosonyezera zili motsindikizidwa mwanthawi zones, zikusonyeza kuti nzotalikitsidwa kwambiri kuziwernga pagulu kapena sizofuna kupeza yankho lake.

Kutsogolera kalasi
 
 

 

 
 
Copyright ©  2023 www.UnitedCaribbean.com. All rights reserved. Disclaimer Click to Contact us