Project Hope     home >>stonecroft>> dongosolo lachikhulpiliro cha stonecroft >> ziphunzitso zambaibulo za stonecroft
ZIPHUNZITSO ZAM’BAIBULO ZA STONECROFT
Women's Empowerment Program
Sports Bible Club
Living Water Bible Club

ZIPHUNZITSO ZAM’BAIBULO ZA STONECROFT

Takulandilani ku Stonecroft ziphunzitso zam’baibulo timapanga mau a Mulungu kufikila aliyese kwa kuwa werengera pomwe ali pa ulendo wawo wauzimu
Tikupemphela ndikuyembekekezera kuti ziphunzitso zimenezi zitsegula mwayi ochuluka kuti inu mukhale ofikapo ndikulimbikitsa kuti muliyike dera lanu kudziwa uthenga wabwino wa Yesu Khristu.

MOWUNIKILAPO

Ziphunzitso za m’baibulo za Stonecroft zinakhazikitsika maka-maka ngati njira yosatilapo pa kufikila kwa m’madera ndi misonkhano. Ziphunzitso zafikila mwakuya ndikugwilisidwa m’ndende, muzintchito, mumipngo ndi m’madera osiyana siyana.

ZOFUNIKILA ZOPENYEKA

Ziphunzitso za m’baibulo za Stonecroft amayesesa kuphatikiza kuutumiki uthenga wabwino umalukidwa kudzera muphunzitso uliwonse la baibulo la Stonecroft

Phunzilo lililonse limakonzedwa ndikuchitidwa mwakuti onse osazoloweleka ndi mau a mulungu angatenge nawo mbali zolumikizilana ku bukhu la mgwirizanowakasindikizidwe ku chipanganop chasopano za mu baibulo lomatsulidwa mu Chiswahili. Kupeleka kuphweka kwa oyamba kumene omwe sanazolowele buibulo kopeza mavesi osiyana siyana mmabukhu amu baibulo

Each study is prepared and conducted so that those unfamiliar with God's Word can participate. Unfortunately many of the women or youth taking part on the studies in Africa will not have their own Bible so page numbers have been removed from the Bible study material and a Bible Verse Handbook has been created in Chichewa with every Bible verse referenced within the Study Book, these have been done in sequential order in each lesson. Obviously if a participant has a Bible then the Bible Verse Handbook is not needed.

Stonecroft Bible Studies are held in homes, workplaces, churches, schools and even outdoors in places like Africa under the shade of a Tropical tree.

It is our aim in the  'Living Water Bible Club', the outreach arm of a   'Drop of Hope' , to demonstrate the love of God by helping communities acquire desperately needed clean water, and experience 'living water'-the gospel of Jesus Christ-which alone satisfies the deepest thirst.

Embedded Microsoft Office presentation, powered by Office.

DAWUNILODI: 'Dontho la Chiyembekezo - Sukulu Polojekitit' Chichewa PowerPoint

'Living Water Bible Club'  will be located in our Drop of Hope School Project located outside of schools, churches and our Africa Goshen Agro Glamping Resorts.

Ziphunzitso za mubaibulo za Stonecraft, mumakomo mmalo ogwilira tnchito , mmatchalichi mmasukulu ngakhale malo apanja mamadera la Africa.

Anazilongotsola kufikila ziphunzitso zapadela ndi mabuku am’baibulo ndipo zimapezeka m’milingo ya ongoyamba kumene nd ozama kwambiri.

Ziphunzitso za m’baibulo za Stonecraft ndizophweka kugwilitsa ntchito m’malo a magulu ang’ono-ang’ononditso mmalo akulu akulu ndipo zimapelekedwa mlingo yosiyana-siyana wamuutali wa ziphunzitso mpaka khumi ndi zinayi.

Ziphunzitso zambiri zili ndi bukhu lotsogolera lotsogoza mtsogoleri kuchititsa ziphunzitso buku lophu8nzilira limagwiritsidwa ntchito ndi wophunzila aliyense payekha.

All Stonecroft Bible studies include a Guidebook for the Guide to facilitate the study. The Study Book is used by each participant along with her Bible or Bible Verse Handbook.

Zokambilana pa gulu ndizofunika kwambiri pakuphunzila ndi kukula pamodzi.

ZOPHUNZILA ZOYENELA

Muziphunzitso za m’baibulo zambiri za Stonecroft wotenga nawo mbali amagwiritsa ntchito bukhu laophunzila ndi baibulo la Swahili Union New Tastament lopezeka ndi a Tanzania Bible Society. Olo mwina kamasulidwe kamasuloidwe kalikose kogwilizana dziko ndi dziko.

Magulu ophunzilawa nthawi zambiri amapezana kamozi pa tsabata pa mphindi zitsanu ndi kamodzi (60min) kufikila mphindi zitsanu ndi zinayi (90min) ngati nthawi ndiyochepa magulu amachiona choyenela kugawa ziphunzitso patheka zokambilana zimachokela mumayankho ogawana kumafunso ochokela m’baibulo a ziphunzitso nditso mukuwelenga kwa malembo.

Mukulitsa utumiki mumadela osiyana siyana ndi utumwi choyenela kuti Gulu liyang’ane njira zochulukitsa mwakuti enatso mumadera athandizidwe muchoonadi cha mau a Mulungu.

KUSANTHULA KWA ZIPHUNZITSO ZA BAIBULO.

Pali njira zitatu za Stonecroft ziphunzitso za mubaibulo ndizo
1. Chiyambi cha ziphunzitso
2. Ziphunzitso za okula mu ukhristu
3. Ziphunzitso zina.

Tikulimbikitsa omwe sanayambe atengapo mbali pa ziphunzitso za Stonecroft kuti ayenela kaye kuyambala ndi chiyambi cha zi[phunzitso Yesu ndi yan? Mulungu ali monga chani? Ndi nzimu woyela alikuti? Ndizoyenela kwa onse ongoyamba kumene ziphunzitso ndi onse ofuna mayankho kwa zikhulupiliro zawo ndi mafutso awo.

Ndondomeko Yophunzirira Baibulo

 
 

 

 
 
Copyright ©  2023 www.UnitedCaribbean.com. All rights reserved. Disclaimer Click to Contact us