Project Hope     home >>stonecroft>>
Stonecroft- Chichewa
Women's Empowerment Program
Sports Bible Club
Living Water Bible Club

BUKHU LA M’MANJA LAZIPHUNZITSO ZAM’BAIBULO LA STONECROFT AFRICA

Welcome to the Africa Stonecroft Bible Studies information E-Handbook. Extracts have been taken, with permission, from the Stonecroft website to create this unique African manual to assist with the training of the African Stonecroft Guides in places like Malawi. Some cultural adaptations have been made to suit the social climate of Africa.

CHOLINGA CHA STONECROFT NDIMASOMPHENYA AWO

Cholinga cha stonecroft ndi utumiki wawo ndi kutengela ndikulimbikitsa azimayi kuti afikile madela awo ndi uthenga wa Yesu Khristu ndi kulemekeza Ambuye Yesu Khristu, ndi kumupanga Ambuye Yesu kudziwika polalika uthenga wa chipul;umutso wa M’baibolo

MASOMPHENYA AWO:

Masompheya a utumiki wa Stonecroft ndikupeleka utsogoleri wapadziko lonse pofikila azimayi ndi Yesu Khristu.

A Stonecroft ndi utumiki wawo amasula azimayi ndi kuwalimbikisa kuti amuziwe Yesu Khristu kwa ena

Kulalikira ndiye gwero lathu. Mongatso kwa utumiki wina uliwonse ndi choncho. Khumbo lathu ndikufikila mzimayi wamsinkhu uliwonse ndi nkhope iliyose ndi uthenga wa Yesu Khristu.

Pemphero ndi maziko ndi nkanamila ya china chili chose timachichita. Yesu anati “ kopanda ine simungathe kuchita chilichose “ Jonane 15:5

Kudalila mulungu kufuna chitsogozo chake, ndiponso mdalitso wake ndichofunika zedi.
Utumwi ndi gawo la dongosolo la utumiki wa uthenga wabwino. Momwe azimayi akukhalira ukristu wake, moti tikupeleka mwayi ndi zipangizo kuthandiza iwo kukula muchikhulupiliro ndiye keneko iwonnso atengele anzawo kuchiyanjano ndi khristu.

Kusula azimayindi utsogoleri ndicholinga chathu china chautumiki wanthu. Kuthandiza azimayi kuzindikila ndi kukulitsa mphatso zomwe mulungu wawapatsa. Kuwazika kuti akhale atsogoleri oyenera omwe angasinthe pakhomo, Mudzi dela dziko lawo, nditso dziko lonse kwa Yesu Khristu.

Zolinga zaziphunzitso zabaibulo za Stonecroft ndizo kulalikila ndi utumwi ziphunzitso zosavuta kulondolazo zammamagulu aang’ono ang’ono zimalimbikitsa moyo wauzimu kuti akule kwa nkhala kale zokhulupilika komano omwe akuphunzila baibolo kumene.

A Stonecroft amagawa uthenga wabwino kwa amayi padzikolonse, ozipeleka oposa 25, 00 osulidwa bwino, nthawi ndi nthawi amayitanila azimayi mdera awo kuti ayambe ubale wawo nd Mulungu wadzikolonse kuzela mwa mwana wake Yesu Khristu.

Wozipeleka mudziko la United States ndiwo mayiko opyola makumi atatu (30) amagwilitsa ntchito zipangizo zofikila za Stone craft ndinso ziphunzitso za baibulo kugawa uthenga wabwino kwa zaka zoposela (75) azimayi a Stonecraft adalira pemphelo ngati chida chotukulila utumiki.

Stonecraft nd bungwe lapadziko lonse, lopanda kuyimila mpingo, ndipotso lopanda zopindula kuchuma.

Mbiri ya Stonecroft
 
 

 

 
 
Copyright ©  2023 www.UnitedCaribbean.com. All rights reserved. Disclaimer Click to Contact us