Project Hope     home >>stonecroft>> atsogoleri amatsogolera>> phunziro lotsogolera buku 1
Kodi Mulungu ndi wotani? - Phunziro #1
Women's Empowerment Program
Sports Bible Club
Living Water Bible Club

Kodi Mulungu ndi wotani?

Purpose of the Lesson
• Begin to understand who God is and what He is like
• Realize that God has always existed and always will
• Accept the Bible as the source of authoritative answers

Help participants become familiar with their Study Book by pointing out the special study helps in the back of their books.

Prayer
Dear God of the Universe, we want to study the Book You wrote because we want to learn about You. Open our eyes, our ears, and our hearts so we can under¬stand the things we read. We come to You in Jesus’ name, amen.

Guide’s Comments
To help us benefit from this Bible study, there are some Guidelines which we will follow. They are located on page 6 in your Study Book.

Ndondomeko yophunzilira

Maphunziro awa ndi mawu a Mulungu omwe cholinga chenicheni ndi kuphunzira zimene baibulo likunena komanso limakhudza bwanji miyoyo yathu. Buku lophunzilira komanso Baibulo ndi zida zokhazo zimene tigwiritse ntchito pamaphunzirowa.

Poyamba tiyankhe kaye mafunso amene ali mu mabuku ophunzilira tisanayambe phunziro liri lonse. Iyi ndi njira yokonzekera phunziro liri lonse zomwenso zipangitse kumvetsa kwa kukambirana kwathu. Tipanga phunziro loyamba limodzi. Maphuzirowa ayamba munthawi yoyikika ndikutha pakati pa ola limodzi ndi ola limodzi ndi theka.

Pakuti tikusiyana kochokera kuphatikizapo matchalichi timverana ndi kulemekeza maganizo ngakhalenso zikhulupiliro za aliyense.

Mmasabata ochepa akudzawa. Tikufuna tiyambe maphunziro atsopano a baibulo kuchokera ku bungwe la Stonecroft. Ganizirani anzanu amene mungawayitanire maphunzirowa.


Who is God? This question has intrigued people for centuries. They have searched deep into history, hoping to unveil “the ultimate controller of the uni¬verse.” They try to discover who God is and understand how He works.

The purpose of these lessons is—
• to learn what the Bible says about God;
• to realize how exciting life can be when we know God and live in fellowship with Him;
• to apply what we learn and develop a deeper, more meaningful relation¬ship with God.

To stimulate our thinking, consider the following:

God Is

The Bible simply states that God is. There is no attempt to prove that He is. There is no great argument or explanation. Anyone who picks up the Bible and reads its first words can know without a doubt that God exists. God, the true and Almighty God, is. He is the One who has caused everything else to come into existence.

Mulungu wakhala alipo,
Ndipo adzakhalapobe!
Kupezeka kwake kwa muyaya kumatchulidwa mwamphamvu
mmawu awiri kuti:

Mulungu Ndi.

How do you react to that statement?. . . . . (Discuss. Acknowledge and encourage their thoughtful responses.)

Mulungu Wamphanvu zonze, opezeka paliponse nthawi ili yonse, amene amadziwa zonse, ali pano.

Adzakhalapobe, chifukwa - Mulungu Ndi.

“Koma opanda chikhulupiliro sikutheka kumkondweretsa, Pakuti iye wakudza kwa Mulungu ayenera kukhulupilira kuti alipo, ndikuti ali obwezera mphotho iwo akumfuna Iye
—Ahebri 11:6

Our New Testaments express the fact that “God is” by using another word instead of “is.”

1. Werengani Ahebri 11:6.(Use your Bible or Africa Bible Verse Handbook) Ndi liwu liti limene lagwiritsidwa ntchito pofotokozera kuti Mulungu Ndi? (exists)

God has always existed and He always will. People exist and you exist. Your physical body has a beginning and an end. But God does not have a beginning or an ending. To say, “God exists” is correct, but to say “God is,” has a more definite meaning. There never was a time when God did not exist. He always was and always will be. Do you see the deeper meaning in the statement “God is” than “God exists?” It is always present tense or now with God.

Mulungu ndi Wolenga

Isanayambike nthawi, kunalibe kathu koma Mulungu yekha mu ukulu wake analipo. Kunalibe kanthu –kunalibe mlengalenga, kunalibe dziko, kunalibe dzuwa, kunalibe mwezi ngakhalenso nyenyezi – kunalibe kathu. Mulungu analankhula ndipo popanda kathu paja panabwera kanthu. Kulenga zinthu popanda zinthu. Chikhalire-Mulungu ndi olenga ndipo palibenso wina.

What do the Old and the New Testament say about God the creator?

2. Werengani mavesi awa ndipo mufotokoze mmene mukumvera mmmawu anu choonadi chenicheni chimene mawu amenewa akuphunzitsa.

Nehemiya 9:6

Akolose 1:15-16

Choonadi chenicheni chimene mavesi amenewa akuphunzitsa ndi: (God is the Creator of all things)

God is the Creator of all things. Genesis, the first book of the Bible, tells us that God spoke things into being. His words are powerful. He spoke and there was light. He spoke and things appeared that never existed before. In fact, all that exists is here because God spoke it into being or, as in the case of humanity, He formed us with His hands. What a wonderful God we have! He created everything that is—out of nothing.

Mulungu ndi wamuyaya

Mawu awiri aku "Mulungu Ndi” akutsimikitsa kuti Mulungu ndi wa Muyaya. Umuyaya ndiwovuta kumvetsa chifukwa cha nyengo imene tikukhala. Ndife akapolo a nthawi. Nthawi imene tinabadwa inalembedwa mkawundula. Ndipo idzakhalaponso nthawi ya kufa, Zimene tikuchita tili ndi moyo, kuyambira pachiyambi mpaka pa kumapeto, zimayesedwa ndi nthawi monga zaka, masiku, maora ndi mphindi. Nthawi zonse timazindikiritsidwa za nthawi imeneyi. Choncho ndikovuta kuti timvetse zakukhala kunja kwa nthawi.

3. Werengani mavesi awa ndi kufotokoza mmene mukumvera choonadi checheni chimene mavesiwa akutiphunzitsa.

(Use your Bible or Africa Bible Verse Handbook)

Masalimo 102:12, 25-27 …. (God is eternal)

Mulungu sayendera nthawi. Alibe chiyambi ndipo alibe mathero. Amakhala mu umuyaya. Sayendera nthawi.

Timakhala mnyengo zitatu - yammbuyo, yatsopano ndi yamtsogolo, Takhala nthawi yam’mbuyo, tikukhala nthawi yatsopano ndipo tidzakhala nthawi yamtsogolo, Mulungu analipo chikhalire ndipo adzakhalapo mpaka kale.

God has no beginning or ending. We had a beginning, but the amazing truth is that we will never have an end! Our physical bodies will die, but our souls and spirits will live on forever.

The Bible tells us in Genesis 2:7 how God made humans to live forever. It says when God breathed the breath of life into the man, he became a living soul.

God made people so they could know Him. That is the purpose of this study—to know God and learn what He is like. In this lesson we have learned that—

  • God is. He has no beginning and will have no end.
  • He is the Creator of everything in heaven and earth.
  • He is eternal—He always has and always will exist.

Another important thing the Bible tells us about God is that He is the only One.

If a response of Question 4 reveals unbelief about there being one God allow the person to give the reasons for the answer. Continue by reading the verses and do not argue.

4. Werengani mavesi awa ndipo yankhani funso lotsatilari. Kodi mukukhulupilira kuti kuli Mulungu mmodzi? Perekani chifukwa mmene mwayankhira.

Yesaya 44:6

Yesaya 45:5

(There is only one God because the Bible says so, and because God says He is the First and Last. There is no other God and never will be.)

Is the Bible True?
Since we have been answering our questions from the Bible, you may be asking yourself why the Bible is a dependable, authoritative resource for our answers.

The Bible writers claimed that they were recording the very words of God. The amazing thing is that, though this is not a claim writers make, the 40 men who wrote the Bible all claim divine inspiration. Over 3,000 times the different Bible writers said, in one way or another, that they were giving people God’s words.

The unity of the Bible is even more amazing when we realize the men who wrote the Scriptures wrote from three continents—Europe, Asia, and Africa. Their writing spread over a period of 1,500 years. They were from different walks of life and wrote in three different languages—Hebrew, Aramaic, and Greek.

The Bible is in perfect harmony from beginning to end—even though it deals with many difficult subjects. Each part needs the other parts to complete the story. The Bible is the complete revelation of how God has provided salvation for all who will believe and receive His wonderful gift.

Mabuku ena a m’baibulo analembedwa ndi aneneri. Awa ndi azitukimiki amene ankanena uthenga wa Mulungu kwa anthu. Amanena zimene zidzachitike mtsogolo ngakhale zaka zochuluka mtsogolomo.

Cholinga cha uneneri mu Baibulo nkutidziwitsa kuti Mulungu alipo ndipo ali ndi cholinga pa dziko lino ngakhalenso anthu. Pakunenera za anthu, malo, ndi zochitika zaka za mtsogolo, Mulungu amakhala akutidziwitsa za cholinga chake pa dziko mtsogolomo. Kupherezera kwa uneneri ndi chitsimikizo kuti Baibulo ndi mawu a Mulungu

In his book Evidence that Demands a Verdict, Josh McDowell gives 61 different prophecies found throughout the Old Testament concerning the birth, life, death, and resurrection of Jesus Christ.1 The New Testament reports the fulfill¬ment of each of these prophecies in detail. We cannot take time to look at all of them now. However, there are two prophecies concerning Christ given in the next two questions.

5. Baibulo limaonekera kudalirika pakuwona kupherezera kwa uneneri.

Mneneri Mika ananenera za malo obadwira a Ambuye Yesu zaka 700 Ambuye Yesuwo asanabadwe.

Mika 5:2
“Koma iwe, Betelehemu Efrata, ndi iwe wamng’ono kuti ukhale mwa zikwi za Yuda, mwa iwe mudzanditulukira wina wakudzakhala woweruza m’Israyeli; maturukiro ace ndiwo a kale lomwe, kuyambira nthawi yosayamba”

Uneneri uwu unakwaniritsidwa pa Mateyu 2:4-6.

Kodi Ambuye Yesu anabadwira kuti? …… (in Bethlehem)

Munthawi yayikulu mchiyembekezero cha Ambuye Yesu, Maria amakhala kumpoto kwa Israyeli ku Nazarete. Betelehem anali kum’mwera kwa Israyeli. Koma boma la a Aroma linalamula kalembera. Aliyense amayenera kubwelelera kwa makolo ake kukalembetsa. Yosefe ndi Maria anali ochokera banja la chifumu la Davide omwe kwawo kunali ku Betelehemu – (1 Samueli 16:1). Malemba anakwaniritsidwa Ambuye Yesu anabadwira ku Betehemu osati ku Nazarete. Ndi Mulungu yekha amene amapanga zithu kutheka. Mulunguyo anatheketsadi.

6. Davide ananenera za kupachikidwa kwa Ambuye Yesu zaka
chikwi Ambuye Yesu aasanabadwe.

Mwachitsanzo, Werengani

Masalimo 22:18
“Agawana zovala zanga, Nalota maere pa Malaya anga.”

Uneneriwu unakwaniritsidwa pa Yohane 19:23-24.

Kodi asilikali aja anapanga chiyani?....

(They divided his clothes into four parts adn because His outer robe was one piece, they threw dice for it)

Uneneri uwu unakwaniritsidwa ndi asilikali a chi Roma amene sanadziwa nkomwe za uneneri wa Chiyuda. Sanakatha kulumikiza ndi munthu amene anangompachika kumene. Ndi Mulungu yekha amene anakanenera zimenezi ndikudziwitsa kuti uneneriwu wakwaniritsidwa.

7. Fotokozani mwachidule zimene Ambuye Yesu ananena zokhudza chipangano chakale. Luka 24:27, 44

The time of the coming of the Messiah, His death, the destruction of Jerusalem, and the destruction of the temple were prophesied in the book of Daniel hundreds of years before they happened. These fulfilled prophecies also confirm the fact that the Bible is a divinely inspired book.

8. Kodi pa 2 Timoteo 3:16 pakuti chiyani za m’mene Baibulo limatitakasira miyoyo yathu?

(All Scripture is inspired by God and is useful for teaching the truth)

Summary
At the end of each lesson, there is a page on which we can make notes. We can use this page to write things we want to remember.

Perhaps, as you study, you would like to make notes about things God wants you to do. On this page, you can also record ideas about how you will apply these biblical truths to your life. It is your page—use it in the way that means the most to you.

For example, we can write some of the things we learned today.

What did we learn about God when we read Hebrews 11:6? . . . . . (God exists or God is)

When we read Nehemiah 9:6, what fact did we confirm?. . . . . (God is the Creator of everything in heaven and earth)

God has no beginning or ending. What is another word that describes His time¬lessness? . . . . . (Eternal)

The Bible repeatedly tells us how many gods there are. How many are there? . . . . . (Only one)

One reason we can believe the Bible is true is that one person who always spoke the truth confirmed the fact that it was true. Who was that person in Luke 24:27?. . . . . (Jesus)

9. Kodi mawu akuti Mulungu Ndi akutanthauza chiyani kwa inuyo pamene mwamaliza phunziro limeneli? … (Accept all answers, but emphasize that God has always existed and always will.)

Next week, Lesson 2 introduces the Weekly Bible Reading. Each day, read the Bible verses that explain more about God and answer one or two questions. Make a note of the new things you have learned about God on the page at the end of the lesson.

In Question 1 of next week’s lesson, you will be asked to write what you see when you think of God. Write the first thing that comes into your mind. Write what is real to you. What or who is God to you?

Some people think that God is—
• a great person far away
• nature
• a power or force in space
• a creator who made us and left us alone
• a bright, glorious light located in heaven
• a patriarch who sits on His throne in heaven and is frustrated by all that is happening on earth

Next week, it will be interesting to hear everyone’s answer to that question.

Pemphero
Atate wa muyaya. Ndikukupembedzani. Ndaphunzira kuti mulibe chiyambi ndiponso mulibe mathero. Ndikuvomereza kuti inu ndi wolenga wamkulu ndipo palibenso wina. Ndikupempha kuti mundithandize kuganiza bwino za Inu pamene ndikuwerenga mawu anu. Ndapempha izi kudzera mudzina la Yesu Khristu. Amen

 
 

 

MULUNGU ALI NGATI CHIYANI?

 
 
Copyright ©  2023 www.UnitedCaribbean.com. All rights reserved. Disclaimer Click to Contact us