Project Hope     home >>stonecroft>> yesu ndani? >>phunziro 5 >>phunziro 6
Stonecroft - YESU NDI NDANI?- Phunziro #6
Women's Empowerment Program
Sports Bible Club
Living Water Bible Club

Ndidzamuona Yesu?

Pemphero

Wokondedwa Atate ku mwamba, Zikomo potiphunzitsa zambiri za chimene Yesu ali.
Tiphunzitseni tidziwe za mbiri kuchokera mu Buku Lanu pamene tikuphunzira phunzirori.
Tikufuna tidziwe ngati tidzamuonadi Yesu. Mu dzina lache, ame.


Kuwerenga Baibulo kwa Sabata:

Werengani gawo la baibulo pansipa ndipo mulembe fundo ya tanthauzo logwira
ntima limene malimva pa kuwerengedwa kulikonse.

Yohane 1:14-18

Yohane 14:1-11

1 Yohane 5:10-12

Mateyu 16:24-27

Afilipi 2:5-11

1 Atesolonika 4:15-18

Yohane 5:24-29

1 a. Yesu ndi ndani kwa inu? . . . . .


b. Kodi Yesu anati lamulo lofunikira kwambiri ndi liti? Mateyu 22:36-40

c. Yesu anachita zinthu zambiri zofunika akanali pa dziko lapansi. Ntchito yofunikira
kwa mbiri ndi chifukwa chimene anabwerera. Chimnali chani? Marko 10:45

2. Lembani mu magawo awa. sankhani ku mau awa:

mlowa malo fuko chosatheka kufa thupi
losachima kubadwa mwa namwali
makumi anayi Mulungu kuikidwa
m'manda kulipira kulamulira chikhululukiro
umuyaya chitatu mtanda mwana
wa nkhosa tchimo

Dipo ........................ analilamula kuti lichitike pa pa anthu ochimwa inali ................... Nthawi
isanayambe, Mulungu anati osalakwa ..................................kufa m'malo a munthu
ochimwa.Anthu amapereka sembe ya nyama yopanda banga—makamaka
....................—akafuna Mulungu kuwakhululukira machimo awo. Mwazi wa nkhosa
umene anaupereka sunachots .......................... Inali chifanizo cha nsembe yoyera imene
Mulungu anayitumiza. Imaphimba tchimo lawo, kufikira Yesu kubwera pa dziko
............................. chifukwa cha machimo a dziko lapansi.

Koma kufa, Amayenera kukhala ndi thupi la munthu ................, chifukwa anali
Mulungu, ndipo kunali ............................ kuti Mulungu afe. Chifukwa chache, anasankha
ndi kukonzekeretsa .................. limene anakonzekeretsa thupi la Iye. ............................ iwo
ku ..........................a dziko lapansi ndikuwapatsa malamulo kuti atsate a kukhala mwa
.........................

Nthawi itakwana, malingana ndi dongosolo Lache, anabwera ku Dziko ngati
Myuda, .............................................. mwana. Anakhala m'moyo ...........................
............................................................. koma pa tskiku ........................Anawuka kwa akufa,
kudzionetsera Yekha anali wa moyo. ataonedwa ndi anthu ambiri kwa masiku
makumi anayi, Anakwera ku mwamba.

Ngongol ..................................younse. Mbali yathu ndi kulandira .................................... cha
Mulungu ndi mphatso ya moyo ..................... Ichi chitanthauza tikulandira imfa ya
Yesu pa mtanda ngati dipo la matchimo athu. Timalola This means that we accept
Jesus Christ’s death on the cross as payment for our personal sin debt. Timalola
Mulungu .........................miyoyo yathu.

Kodi chifukwa chani ndikofunika kuti wina aliyense adziwe zinthu izi? ndizofunika chifukwa chikhulupiriro chmapanga chikhalidwe. Chimene timakhulupirira chimapanga chimene timachita ndi m'mene timachitira. Chifukwa chake ndikofunika kukhala ndi kumvetsetsa kwa bwino za chimene Yesu ali.

Chikhulupiriro chimaumba Chikhalidwe.

3. Yesus akabwera msogolo, adzamuone ndani? Chibvumbulutso 1:7

 

4.Baibulo limati kudzakhala nthawi ya masautso ndi chizunzo pa dziko la pansi.
Werengani zimene zidzachitike pa dziko Yesu asanabwerenso, ndipo mulembe
zimene zakupatsani chidwi powerenga izi.

a. Mateyu 24:21-31

b. Marko 13:32-37

c. Luka 21:25-28, 34-36


5. Kodi chimachitika n'chiyani munthu akamwalira? Ahebri 9:27

6. a. 2 Akorinto 5:10

b. Machitidwe 17:30-31

c. Chibvumbulutso 20:11-15

Anthu akamakamba za kupulumutsidwa, amakamba za kupulumutsidwa ku chilango chosatha mu nyanja ya moto.

Tikamawerenga za chimene Mulungu amanena za chiwerezo chache cha chilungamo, timazindikira kuti kulandira Yesu kumatipulumutsa ife kuchilango chotiyenera. Tikuyenera kukhala ofuna kudzipereka mwathunthu kwa Iye. Mitima yathu ikhale yodzala ndi matamando kwa Iye pa chipulumutso chake chachikulu!

Mulungu safuna alo munthu m'modzi apite ku gahena. Iye anapangira gahena
kukhala ya satana ndi amithenga ake.—osati anthun (Mateyu 25:41). Anthu ali
omasuka kusankha Mulungu kapena satana.

Khalani mukudziwa za Umuyaya!

7 a.Kozi zimene maphunzira zikupindura chani pa moyo wanu wa tsiku ndi tsiku?
2 Akorinto 7:1

b. Kodi maonedwe anu pa zakukhala ndi zinthu ndi zimene mukulingalira mutatenga ndi kukhala nazo asintha motani? Mateyu 6:19-21

c.Kodi zoti Mzimu Woyera akukhala mwa okhulupirira zimathawathandizira bwanji m'maonedwe awo pa za ziphinjo ndi zokhumudwitsa? Yakobo 1:2-4

d. Kodi chidziwitso cha dongosolo la Mulungu chikuyenera kuchita chani pa maonedwe a okhulupirira pa za kugawa uthenga wabwino kwa wena. 2 Timothy 4:1-5

e. Kodi 1 Akorinto 15:58, amalimbikitsa bwanji okhulupirira kuti akhale wamachawi mu ntchito ya Mulungu?


8. Maphunziro a Mau a Mulungu amasintha miyoyo. Maphunziro awa akusinthani
bwanji myo wanu?

9. Lembani pemphero kufotokozera mathokozo anu kwa Mulungu potumiza Mwana
Wake, Yesu Khristu. Pazokambirana, mudzakhala ndi kusankha kogawa pemphero
lanu. Lembani pempher lanu apa.


Pemphero Lotsekera

Tate wathu wakumwamba, zikomo chifukwa chobwera pa dziko kudzatifera, zikomo chifukwa chobwera pa dziko mkudzadzitengera chilango machimo athu. Zikomo polola kukhala m'moyo wathu. Zikomo chifukwa cha lonjezo simudzatisiya tokha! Tithandizeni kupereka miyoyo yathu kuti uilamulire. Malizani zimene mayamba m'moyo wa wina aliyense. Tapemphera mu dzina la Yesu, Ameni.

 
 

 

YESU NDI NDANI?

 
 
Copyright ©  2023 www.UnitedCaribbean.com. All rights reserved. Disclaimer Click to Contact us